lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu namadingo – linny hoo chalamanda

Loading...

linny hoo
linny hoo
uyu linny lero mwana ameneyu
mwana wa nzeru

linny hoo (linny)
linny hoo
uyu linny lero mwana ameneyu
mwana wa nzeru
kukacha m’mamawa ah ah
amatenga tchache
kusetsa pakh0m~
pakh0m~ pa mayi wache

kukacha m’mamawa (early morning)
amatenga tchache
kusetsa pakh0m~
pakh0m~ pa mayi wache

makolo a linny ( eti makolo a linny)
amuyamikira
akuti linny lero mwana ameneyu
mwana wa nzeru

makolo a linny (makolo a linny)
amuyamikira
akuti linny lero mwana ameneyu
mwana wa nzeru
linny
linny hoo
linny hoo
linny hoo
uyu linny lero mwana ameneyu
mwana wa nzeru

linny hoo
linny hoo
uyu linny lero mwana ameneyu
mwana wa nzeru

agide gogo wa namadingo
amuyamikira
akuti namadingo mwana ameneyu
mwana wa nzeru

a gide gogo wa namadingo
amuyamikira
akuti namadingo mwana ameneyu
mwana wa nzeru

simikunamana agogo
nthawi zina ine (nthawi zina)
ndimalota ine
bambo anga atandisiya
ndasala ndekha
nthawi zina ine (nthawi zinane)
ndimalota ine
bambo anga atamwalira
ndasala ndekha

nkhondo amama (nkhondo amama)
nkhondo amama mwe (nkhondo amama mwe)
nkhondo amama chalamanda
ozafera moyenda we

nkhondo amama hiii
nkhondo une amama wee
nkhondo amama chalamanda
ozafera moyenda we

ndang’ovya mbiriyo
mbiriyo
mbiriyo mwaona lero

ndang’ovya mbiriyo
mbiriyo
mbiriyo mwaona lero

agiddes ayimba eh
ayimba eh
zokomatu mwaona lero
ndipo chalamanda ayimba eh
ayimba eh
zokomatu mwaona lero

ndamva kuti mwakwatira
mwabala mwana woyera
dzina lake musolo eh

munamva kwa ndani
kuti mwakwatira

ndamva kuti mwakwatira
mwabala mwana woyera
dzina lake musolo eh

mnangopanga unkhoswa ukwati
nzakuyitanari

musolo eh (eti musolo eh)
musolo eh
musolo mayi

musolo eh
musolo eh
musolo mayi

mwana ameneyi ndi naayi ake
ndikufuna ndipite nawo ku uk
mwana ameneyi ndi naayi ake
ndikufuna ndipite nawo ku uk

maphunziro onse onse
akaphunzire ku uk
maphunziro onse onse
akaphunzire ku uk

ndamva agogo ndamva
koma timiyeko che meri
che meri kunali che meri

che meri ummm
che meri ummm
che meri
kunali che meri

che meri mama mwe
iya meri mwe
iya darlie
kunali che meri

hiiiyo iya meri mwe
iya darlie
kunali che meri

timbiyepo hakoma paja
hiiiyo iya meri mwe
iya darlie
kunali che meri

akafuna kunena kuno
agiddes agiddes agiddes agiddes
inu abwana tabwerani kuno

akafuna kunena kuno
chalamanda chalamanda
chalamanda chalamanda
inu abwana tabwerani kuno

akafuna kunena kuno
agiddes agiddes agiddes agiddes
inu abwana tabwerani kuno

zinali choncho nthawi ya napolo
napolo hiii wachabe
napolo hiii wachabe
wachabe

napolo wachabe
napolo wachabe

wateng’a ing’alamu
kukataya k~mching’a
kutuma akaida kukatola
pobwera adona nahra mayiwe

wachabe
napolo wachabe
napolo wachabe

timalize ndi buffalo soldier
buffalo soldier
buffalo to america

buffalo soldier
buffalo to america

when i was a young boy
i dreamed to there in america
when i was a young boy
(ngati ine ka young boy)
i dreamed to there in america

oyiyoi yoiyo
oyiyoi yo
oyiyoi yoiyo

oyiyoi yoiyo
oyiyoi yo
oyiyoi yoiyo

if i had much money
i go to sing in america
if i had much money
i go to sing in america

oyiyoi yoiyo
oyiyoi yo
oyiyoi yoiyo

oyiyoi yoiyo
oyiyoi yo
oyiyoi yoiyo


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...