lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu praise umali – plan

Loading...

[verse 1: praise umali]

i worried all the time
i thought i’m running out of time
can’t take it a day at a time sometimes

man our dreams have been too loud since
we were only young kids
and now, we grown they loud still

i know ndizambiri umafuna mtima
nde pena mantha ankadzandigwila
like what if we don’t make it (yeah yeah)
what if we don’t make it (yeah yeah)
[chorus: praise umali]

koma tachoka nkutali
mulungu ~n~li ndi pulani
pulani

inu zonse ndi nthawi
mulungu ~n~li ndi pulani
pulani

yopanga za ifeyo (oooh oooh oooh)
yopanga za ifeyo
akupanga za ifeyo (oooh oooh oooh)
akupanga za ifeyo

[verse 2: gwamba]

yoh
venue yomweyo ena amaflopa
samatrenda nyimbo zawo akadropa
nde pena pride imafuna idzindikopa
koma mbuye w~nga sangakondwe kuti nzizipopa

nde rule number 1, k~makhala humble
poti ukazikweza amasiya kupanga zako
rule number 2, osakhala ndi tsankho
poti lero ndi kape mawa ali pamwamba pako
nkayang’ana k~mbuyo ngati ndingokuwa mbuye
ndinakhonza chani kuti inu mundimasule
mwandichotsa kutali kwinakunso mulambule
ulendowu ndiwautali koma

[chorus: praise umali]

koma tachoka nkutali
mulungu ~n~li ndi pulani
pulani

inu zonse ndi nthawi
mulungu ~n~li ndi pulani
pulani

yopanga za ifeyo (oooh oooh oooh)
yopanga za ifeyo
akupanga za ifeyo (oooh oooh oooh)
akupanga za ifeyo


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...