lirik lagu mufrika – kumpeta milombe
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwathela alumbwana
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwathela alumbwana
kuzebenza tisebenza bwino
ndalama timapeza
koma potsilizira pake eeh!
tinali nao anzathu
tinali kuseka nao
tinali nao astikana
odsziba kusamba bwino
nanga lelo alikuti
ambuye mwatisiyiranji
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwsila alumbwana
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwasila alumbwana
iyi nthenda niyoipa
ndiponso siyimasankha
imagwira aliyense
kuyambira kubana mpaka makolo
koma anyamata ndi astikana
nibame bakula maningi
nangatu tizakhala bwanji
popeza ndiye tsogoro
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwathela alumbwana
ooh ku mpeta milombe
kwathela ayamata ooh
ku mpeta milombe
kwathela alumbwana
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu arlene harden – he’s a good ole boy
- lirik lagu scar symmetry – digiphrenia dawn
- lirik lagu pharman58 – allright
- lirik lagu jrk 19 – mec de panam
- lirik lagu yuniiorr – intro
- lirik lagu joe may (usa) – the queen’s wino
- lirik lagu j. embi – third eye open
- lirik lagu anabela pires – a minha vida vai começar
- lirik lagu fresh oil and chips – girlfriend things
- lirik lagu fuhmahj – kamugachi