lirik lagu mistah yemie – musamukwatilise
yemie music on the track
[intro]
tings are not tswai
tings are not tswaaa
aaa ayii
ajawa you know oooii
mistah yemie on it
[verse 1]
takharani pansi abambo a rabecka
zomwe ndikambe zuyenera kuveka
ndudziwa ndinu ovuta muyenera kudekha
musaphwekese iyi sinkhani yophweka
mwana wanuyu nde tsono ndiw~ng’ono
zomwe mukupanga zitha k~muphera tsogolo
mukuti amare chosecho ali form folo
zimene mukupanga sizoyenera pa kholo
akukwidzingani nde musapange makani
mukuti amare kufera bread ndi bun
mtima wanu ndiotani
ndinu m’dala otani
zomwe mukupangazi azakulozesani gun
[chorus]
chabwino tikupenpha tagwada tikuchondelera
”aaaaaaa aaa aaah”
ngati ma nearby sitikuyenera kuonelera
”eeeeee eee eeeh”
musamu kwatilise eeeh
”aaaaaaa aaa aaah”
musamu kwatilise eeeh
”eeeeee eee eeeh”
[verse 2]
ndilibe nazo kaya zachokera k~mpingo
kaya wina wake watopa kukhara single
nde basi mwaganiza mungokwatlisa mwana
kaya mukufera poti munthuyo ndi bwana
dziwani kuti malamuro sakulora
you hafi think about the future osafera dollar
mukupangazo muzangoonongesa mwana
ichi sichikondi m’dala sangafile mwana
k~manamizira simungakwanitse fee’s
koma chonsecho muk~mangura ma jeans
kukhalira pachiwaya muk~makana beans
ngati uli umbuli eeeh munamaliza
[chorus]
chabwino tikupenpha tagwada tikuchondelera
”aaaaaaa aaa aaah”
ngati ma nearby sitikuyenera kuonelera
”eeeeee eee eeeh”
musamu kwatilise eeeh
”aaaaaaa aaa aaah”
musamu kwatilise eeeh
”eeeeee eee eeeh”
[bridge]
yoo
izi zikuchitikabe m’mamidzi ndi m’milaga
koma ndiudindo wa wina aliyense
kuti tithetse mchitidwe umenewu
[verse 3]
mwana wanuyu nde tsono ndiw~ng’ono
zomwe mukupanga zitha k~muphera tsogolo
mukuti amare chosecho ali form folo
zimene mukupanga sizoyenera pa kholo
akukwidzingani nde musapange makani
mukuti amare kufera bread ndi bun
mtima wanu ndiotani
ndinu m’dala otani
zomwe mukupangazi azakulozesani gun
[chorus]
chabwino tikupenpha tagwada tikuchondelera
”aaaaaaa aaa aaah”
ngati ma nearby sitikuyenera kuonelera
”eeeeee eee eeeh”
musamu kwatilise eeeh
”aaaaaaa aaa aaah”
musamu kwatilise eeeh
”eeeeee eee eeeh”
chabwino tikupenpha tagwada tikuchondelera
”aaaaaaa aaa aaah”
ngati ma nearby sitikuyenera kuonelera
”eeeeee eee eeeh”
musamu kwatilise eeeh
”aaaaaaa aaa aaah”
musamu kwatilise eeeh
”eeeeee eee eeeh”
[outro]
yemie music on the track
[intro]
tings are not tswai
tings are not tswaaa
aaa ayii
ajawa you know oooii
mistah yemie on it
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu bernhard brink – keinen millimeter zwischen uns
- lirik lagu christ dillinger – russel westbrook
- lirik lagu tiredboy – обессилен (exhausted)
- lirik lagu john wesley harding – meet the sheep
- lirik lagu eliza mclamb – salt circle
- lirik lagu vanessa amorosi – baby’s on ice
- lirik lagu кажэ (kaje) – лёд тронулся (the ice has moved)
- lirik lagu tercer nivel – hoy (en vivo)
- lirik lagu ace og – like woah
- lirik lagu lucyv – summer madness