lirik lagu lawi – chifundo nane
[intro]
ayy
chifundo nane
chifundo nane
oh, chifundo nane
chifundo nane
chifundo nane
chifundo nane
mtima w~nga don’t you worry
everything is gonna be alright
[chorus]
ambuye ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
mtima w~nga sudera nkhawa
chif~kwa ali ndi chifundo nanee
ine mtima w~nga sudera nkhawa (oh no)
chif~kwa ali ndi chifundo nane
[verse 1]
machimo anga ndi ambirimbiri osawerengeka ndipo
mutazindikira zamumtima mw~nga mukhoza k~mandisala
m~th~ kufuna kundimangilira ndikundiponya mu m’ndende
ndizokoma kundiweruza, nzovuta kundimvetsetsa
ndiye amene anandipanga amandidziwa
zinsinsi zangazi pamaso pake ndizosabisika
koma ngakhale ndimachimwa iye andikondabe
amatsegura manja ake ndi kundik~mbatira
[chorus]
oh, ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nanе
mtima w~nga sudera nkhawa
chif~kwa ali ndi chifundo nanee
ine mtima w~nga sudera nkhawa (oh no)
chif~kwa ali ndi chifundo nanе (oh, yeah)
[verse 2]
ayi~yayi~yayi
ayi, ndachoka kutali, moyo w~nga ndi umboni
wandimenyera nkhondo, ndangokhala chete
pomwe adani anga andik~mbira mitsinje
wandimangira mlatho, ndayenda powuma
wandifewetsera zolimba zanga
[chorus]
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ali ndi chifundo nane
ine mtima w~nga (sudera nkhawa chif~kwa ali ndi chifundo nane)
ine mtima w~nga (sudera nkhawa
chif~kwa ali ndi chifundo nane)
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu yung tk – rose gold
- lirik lagu ej michels – end of the night
- lirik lagu 林二汶 (eman lam) – 在你身旁 (partnering)
- lirik lagu blackberry smoke – you hear georgia
- lirik lagu crymode – i remember
- lirik lagu teejayx6 – allah 2
- lirik lagu freddy vorobev – i’m looking for my love
- lirik lagu tacica – 贅沢な蝋燭 (zeitaku na rousoku)
- lirik lagu nvcaine – sakura
- lirik lagu 星歴13夜 (seireki13ya) – 箱庭 (miniature garden)