lirik lagu langwan piksy – mpaka udzipita
ndikudziwa kuti ndafika mammawa
ndikudziwa zaku bhowa
yeah mtima wako ukuwawa
koma babe ukudziwa za ku bhawa
ndimakupeza wagona
sticheza ngati banja
ine ndimakhala ndatopa
lonseli ndi vuto langa
mammawa uliwonse uk-malira
lero ndakupeza ukupakila
komano honey just hold on
i know i’ve done wrong
komazi ndi zazing’ono
nde
chorus
mpaka udzipita
sindufuna kusikidwa.
zomwe ukufuna ine ndzichita ndikwanitsa
yes i know i didn’t give you much attention
lately
every time on the cellphone
too much what’sapp, too much twitter
umafuna kundikonda koma sinkupasa mita
busy ntchito weekend ndi anzanga
ndimalonjeza zinthu zochuluka simpanga
umadandaula koma mmaiwala nsanga
kuchitenga for granted chikondi chomwe umandipatsa
mmalo molowera mmwamba i know we going down
ndikale lomwe ndinayenda nawe mtown
komano honey just hold on
i know i’m doing wrong
komazi ndi zazing’ono
nde
chorus
mpaka udzipita
sindufuna kusikidwa.
zomwe ukufuna ine ndzichita ndikwanitsa
usayese ndikutenga simple
kwa ine utanthauza dziko
chikondi chako chindipasa dzitho
ndikamati ndine mphongo ndiwe
i swallow my pride ndameza matama
ndameza zochuluka pa kamoz
ndatsamwa
ndiri ndi munda koma sinkupalira
ndikudziwa sukukondwa mmomwe zikukhalira
ndiwauza anzanga ino weekend
sindioneka poti ndikhala ndiwe
eh yah ndikhala ndiwe baby
sindilora upite
chorus
mpaka udzipita
sindufuna kusikidwa.
zomwe ukufuna ine ndzichita ndikwanitsa
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu raksasa – diculik ke surga (feat. bonita)
- lirik lagu hidden message – awal yang baik
- lirik lagu ebith beat a – masak
- lirik lagu lauren aquilina – low
- lirik lagu the fix – home
- lirik lagu monsta x – hero
- lirik lagu monsta x – gone bad
- lirik lagu sunscreem – when
- lirik lagu dove cameron – if only
- lirik lagu austin mahone – not far