lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu wxll stephens - coca cola

Loading...

verse i
mwina sumadziwa lero udziwe
mwina sumafila lero ufile
kachikondi kakoko undifilitse
mahope angawo iwe undigwiritse eh eeh!

hook
pano ndimangomwa coca cola (coca cola)
pano ndimangomwa coca cola (coca cola)
mowa ndinasiya pano coca cola
ndimangomwa, coca cola
coco coco, coca cola
mmhhh!

verse ii
everytime
everytime i see you i dey crave for coca cola x2
kodi unandita~ani
unandipanga chani
kodi unandita~ani
unandioanga chani
babe unandita~ani
unandipanga chani?

refrain
mwina sumadziwa lero udziwe
mwina sumafila lero ufile
kachikondi kakoko undifilitse
mahope angawo iwe undigwiritse eh eeh!
hook
pano ndimangomwa coca cola (coca cola)
pano ndimangomwa coca cola (coca cola)
mowa ndinasiya pano coca cola
ndimangomwa, coca cola
coco coco, coca cola
mmhhh!

verse iii
so many things i could do that includes stopping alcohol just to be with you x2
ndiwe mamacita
usanabwere ineyo mnali vendetta
kodi mamie ukundimva?
come closer osandipatsa meter

hook
pano ndimangomwa coca cola (coca cola)
pano ndimangomwa coca cola (coca cola)
mowa ndinasiya pano coca cola
ndimangomwa, coca cola
coco coco, coca cola
mmhhh!


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...