lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu trappy beats - cardio

Loading...

[intro: trappy beats & cizzle]
aseh! trappy
ay
ay, ay
eya, eya

[verse 1: trappy beats & cizzle]
ngini ili sharp taphusha
ndi boys yanga ija tikalinka
timaichemesa ife tikafika
timasiya nkhani ife tikadusa
ngini ili sharp taphusha
ndi boys yanga ija tikalinka
timaichemesa ife tikafika
timaichemesa ife tikafika
tikupanga udolo
boys yamenya call
tatipeze chapa chanco
tagwetsa kale mabotolo folo
tikupanga udolo
boys yamenya call
tatipeze chapa chanco
tagwetsa kale mabotolo folo

[chorus: cizzle]
tikuphusha ngini khala ngati cardio
tikusuntha tryna get money ngati sadio
on another level
nyimbo zathu munvela pa radio
cerebrity status, ma hater outside
ali panja
[post~chorus: trappy beats.]
koma tikangofika patentha, patentha
pachema, pachema
koma tikangofika
patentha, patentha
koma tikangofika
pachema, pachema
koma tikangofika
patentha, patentha

[bridge: trappy beats]
tikafika kuchema kuno, kuchema kuno
tikafika kuchema kuno, kuchema kuno
ah! tikafika
ah! tikafika
ah! tikafika
ah! tikafika

[chorus: cizzle]
tikuphusha ngini khala ngati cardio
tikusuntha tryna get money, ngati sadio
on another level
nyimbo zathu munvela pa radio
cerebrity status, ma hater outside
ali panja
[post~chorus: trappy beats.]
koma tikangofika patentha, patentha
pachema, pachema
koma tikangofika
patentha, patentha
koma tikangofika
pachema, pachema
koma tikangofika
patentha, patentha


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...