lirik lagu temwah - malawi (zakwathu)
[verse 1]
m~a lawi~lawi
malawi, ndati~ndati
timadya nkhwani wa mati~mati
kuphika thobwa la khati~khati
ku malawi, manganje
yamba kuvina usathawe
ku nsanje, mwa chaje
chi sena chiyankhulo chake
tikafuna utaka, sitichita kusaka
lake malawi is blessed with some beautiful fish (beautiful fish)
tikafuna utaka, abale sitichita kusaka
lake malawi is blessed with some beautiful fish (beautiful fish)
[chorus]
chikhalidwe’chi nchakwathu
chiyankhulo’chi nchakwathu
mavalidwewa ngakwathu
mavinidwewa ngakwathu
chiyankhulidwe nchakwathu
mayankhulidwe ngakwathu
ngakwathu…
[verse 2]
kukacha mamawa
timapita k~munda, kukalima
zolima zija ha
sitisiyila pompo, kupalira
nanga udya bwanji osalima?
ulemera bwanji osavepa?
nsanje, mtima osadekha
kukhala ndi anthu nzosatheka
tisanimizane makosana
hard work pays, never fails a dream
galu okuda suzamuona
alendo nawo sasowa chotola
anthu ake ngasangala
timalandira anthu mwansagala
uku tikuchezelana nthabwala
dziko lathu la uchi ndi mkaka
[chorus]
chikhalidwe’chi nchakwathu
chiyankhulo’chi nchakwathu
mavalidwewa ngakwathu
mavinidwewa ngakwathu
chiyankhulidwe nchakwathu
mayankhulidwе ngakwathu
ngakwathu…
chikhalidwe’chi nchakwathu
chiyankhulo’chi nchakwathu
mavalidwewa ngakwathu
mavinidwewa ngakwathu
chiyankhulidwе nchakwathu
mayankhulidwe ngakwathu
ngakwathu…
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu dazaro - blackout
- lirik lagu anbu monastir - du bist meine hinata
- lirik lagu veason - paranoje
- lirik lagu ung-skab - du vil ik se (føler den ik)
- lirik lagu nicholas craven & boldy james - power nap
- lirik lagu hozwal, marcianeke & tunechikidd - déjate llevar
- lirik lagu m.i abaga - the hate
- lirik lagu tau tau טאו טאו - קוקו
- lirik lagu titan - gira
- lirik lagu star seed, aaron shirk, & psyb3r - alone