lirik lagu suffix (mwi) - kwanu nkwanu
[intro:]
listen
[verse 1:]
bambo anga ankandikhazika
pansi, ndili mwana wovuta
ndili chakusekondale heee ndisakuganizaso zoyimba
mwana w~nga ndithu kukula
ife taonapo yambili mvula
ndiwe first born ife tikudalila, ukafuntha uzapita mwachangu k~manda
kusukulu komwe uliko, uzik~mbuka komwe uchokela
nanenso nnali ndiazizanga ambili sindziwa komwe ~n~lowela
[chorus:]
dziwa dziwa dziwa, mwana w~nga
dziwa dziwa dziwa, mwana w~nga
dziwa dziwa mwana w~nga
dziwa dziwa, mwana w~nga
kwanu nkwanu nkwanu
mwana w~nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w~nga, kwanu nkwanu
mwana w~nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w~nga
heeehhh
[post~chorus:]
hee huhu
hee huhu
hee huhu
hee huhu
[verse 2:]
yea, life sikhala fair
macritisism sabweletsa sheda
aliyense ali nzokonda zake, akadana ndizokonda zako usamawatengela
k~masiyanitsa azako ndiabale
ena utavutika sangathandize m’bale
osamatengeka akamakuchemelera
enawo ukazazizila azakupanga chandamaleee
[chorus:]
dziwa dziwa dziwa, mwana w~nga
dziwa dziwa dziwa, mwana w~nga
dziwa dziwa mwana w~nga
dziwa dziwa, mwana w~nga
kwanu nkwanu nkwanu
mwana w~nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w~nga, kwanu nkwanu
mwana w~nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w~nga
heeehhh
[post~chorus:]
hee huhu
hee huhu
hee huhu
hee huhu
[outro:]
dziwa dziwa dziwa, mwana w~nga
dziwa dziwa dziwa, mwana w~nga
dziwa dziwa mwana w~nga
dziwa dziwa, mwana w~nga
kwanu nkwanu nkwanu
mwana w~nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w~nga, kwanu nkwanu
mwana w~nga, kwanu nkwanu nkwanu
mwana w~nga
heeehhh
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu raiashi - yokohama
- lirik lagu jeune morty - atm
- lirik lagu ava elay - eternity
- lirik lagu fallencastle - protect!
- lirik lagu ghxstwraith - paranoid
- lirik lagu jawis - no lie
- lirik lagu seiji oda - [to the earth.m4a]
- lirik lagu стань (staniy) - рыцарь грозы (knight of the thunder)
- lirik lagu boom boom kid - tiro al blanco
- lirik lagu hoodbaby skarr - cash app*