lirik lagu suckle - osaopa part 3
intro
kugona kudzuka osalota hehe
verse 1
ndikayamba ndi moni sindimawedza kwakuya//
mumazitenga za nthabwala sindimapindula//
paja ndi mwazi okha moyo w-nga anagula//
pano nzeru zanga zonse zathera mukabudula//
ndakhumudwa ntava ena anakachitabe mantha//
ali ndi kamwa la prayer kuthekera kosatha//
mfumu yawo silephera akuchedweranji nanga//
malo mogwetsa mawondo ndikuyang’ana mmwamba//
zochita mantha zik-n-lipo munakatsatabe dziko//
kod zonguopa zongutengana mof–ka tele pano iwo ankoka//
abu kozeka niotopa//
hmm sitisekerera mkango pali nkhosa(nkhosa!!)//
maganizo anyambuti mukutsutsa(tsutsa!!)//
chilungamo chimawawa siti hater//
koma zina mumalalikira inu ndizopeka//
osaopa part 3 ndiya mdidi//
sikuti muli faith mussa sinampange ft//
kubakira chilungamo tikupangani defeat//
kma adha imagine people calling someone a spiritual father//
aah but understand it’s so disgusting father ndiwammwamba//
hook
ndinasintha(eeeh!!)ena akudabwa(eeeh!!)//
ati tufuna potchukira tawathira gaza(aah)//
ati sitinafike pobakira chilungamo//
pano tasanduka opusa akakaka nde kawabaya//
koma iwe osaopa ine osaopa//
olenga dziko amadziwa zaifeyo osaopa//
koma iwe osaopa ine osaopa//
nkhani ndi treasure tikuyisaka ifeyo!!//
verse 2
aah ka part 3 kabwera ngati remake//
olo soja uno man samayembekezera eeh//
ena maganizo anu mmati mwina ndipala eeh?//
ayi njee uwu si moto iyi ndi word of god//
mantha aja alik-mpoto ndikuwaphika pot(i)//
bola asalire sindikuopa//
inuso mu(t)salire akusiya yehova//
timajoke pambali uziva word osati style//
muziyamikira ndapha nyimbo kutha osapindula//
ati black flame david osaopa yawo anak!ller//
malo moti muziti osaopa yawo anapreacher//
kuchedwa ndima compare instead of getting the word//
ndilibe mantha braza mphamvu nde anandipatsa//
zotchedwa mwana wake ena ake atamanda//
akwezeka dzina lake hosanna nde ayimbidwa//
glory to the most high father in heaven//
mwayenera matamando ifeyo tichepe//
kulemekeza dzina lanu ifeyo tisaleke//
koma preaching the truth mawu anu afalike//
go into the world and preach the gospel//
anatisiyira izi he even defeated ka death bruh//
ndiye ndilekenji munandisintha ndinu(ayi!)//
ngati mukuopa ife t-tsate inu (ayi!!)//
kw-ngulekani kunsaka munthu olukamba chilungamo inzo nzako//
hook(x2)
ndinasintha(eeeh!!)ena akudabwa(eeeh!!)//
ati tufuna potchukira tawathira gaza(aah)//
ati sitinafike pobakira chilungamo//
pano tasanduka opusa akakaka nde kawabaya//
koma iwe osaopa ine osaopa//
olenga dziko amadziwa zaifeyo osaopa//
koma iwe osaopa ine osaopa//
nkhani ndi treasure tikuyisaka ifeyo!!//
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu małyksiążę - oczy
- lirik lagu boba dread - минус плюс (remastered) (minus plus - remastered)
- lirik lagu robert finley - let me be your everything
- lirik lagu balzac - black sunday
- lirik lagu nineteen ninety four - hedgehog's dilemma
- lirik lagu akapellah - gordo funky
- lirik lagu hateful decay - manifestation
- lirik lagu marshmello - silence (lost kings remix)
- lirik lagu macanache - jon cel mic
- lirik lagu dark dagger - love is a bitch