lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu suckle - lord i know

Loading...

intro(hazel)

ooo yeh yeh! lord i know i know oo!
when i feel the pain i put it in heart
lord i know lord i know ooo!!

hook(suckle)
x2
lord i know,i know(please don’t k!ll my vibe!)
i know, i know(world of sin no lie!)
when i feel the pain,i put it in heart
when i feel the pain,i put it in hearttt!
.
.
x2
helelele! helelele! ndinganene bwanji?
nyengo wasinthayi mwandichoketsa kutali

verse 1(suckle)
lero sindiyambaso ndi moni//
nzosachedwa w-nga ndi umboni//
galu opanda nchila opusa//
walandira mkango wa yuda mofasa//
kuchimake kogonjetsa imfa kuyipatsa 3 days osadutsa//
mbuye inu nokha ndipatali//
simusankha olo ndili mphawi//

bridge (queen reg)
mukhale nane nthawi zonse/
ndikaputhwa mumandiwutsa//
vulu wanu nimwe u never fail//
hakuna kamawewe!! /

hook(suckle)
x2
lord i know,i know(please don’t k!ll my vibe!)
i know, i know(world of sin no lie!)
when i feel the pain,i put it in heart
when i feel the pain,i put it in hearttt!
.
.
x2
helelele! helelele! ndinganene bwanji?
nyengo wasinthayi mwandichoketsa kutali

verse 2(suckle)

vera mwana w-nga vera khutu lako tchera dziko osalivera//
amapita patali ndi omwewa omwe anatsata yemwe anawafera//
nkhondo yamumtima siyazida//
dalira yesu mphw-nga siyazida//
tanyozera mawu ake siyazida//
.
.
. (queen reg)
usanyozere mawu ambuye//
iye ndi aphor and omega//
amakhala nafe satisiya tokha//
.
.
(suckle)continuing
lord i know!
ndakula mutu sichilema no! //
ndagoma nanu pamabombono//
ndadza mogonja sizankhondo no//
nyengo wasinthayi siya weather kuti mwina zachitika may//
kugwa ndikudzuka pena nkhani yake simakhala revenge//
muzabwera ngati mbala eya after tenant kukanika fee//
range ili pano ndiya intensive tipangenikoni free//

hook(suckle)
x2
lord i know,i know(please don’t k!ll my vibe!)
i know, i know(world of sin no lie!)
when i feel the pain,i put it in heart
when i feel the pain,i put it in hearttt!
.
.
x2
(hazel)
ndinganene bwanji?
nyengo wasinthayi mwandichoketsa kutali


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...