lirik lagu sevenomore (mw) - my malawi
[chorus]
amangolira (mayi malawi)
walira (mayi malawi)
amangorila (mayi malawi)
walira (mayi malawi)
amangoti (ayi~ayi~ayi~ayi, ayi~ayi~ayi~ayi~ayi)
ana anga inu
ana anga inu
amangoti amangoti (ayi~ayi~ayi~ayi, ayi~ayi~ayi~ayi~ayi)
ndikuvutika ndikuzuzika inu mulipo
[verse 1]
taonani ndinakupatsani kamoyo kabwino, kokongola
inu taonani ndinakupatsani tiana tabwino, tokongola
koma nokha nokha
muk~maphana
muk~malimbana
muk~matembelerana
muk~maponderezana
simukukondana
muk~masalana
muk~matamba
chosecho manune (mayi wanu ine) kachitenje ndikamozi
kamalaya ndikamozi
ka burangete ndikamozi (yah)
[chorus]
amangolira (mayi malawi)
walira (mayi malawi)
amangorila (mayi malawi)
walira (mayi malawi)
amangoti (ayi~ayi~ayi~ayi, ayi~ayi~ayi~ayi~ayi)
ana anga inu
ana anga inu
amangoti amangoti (ayi~ayi~ayi~ayi, ayi~ayi~ayi~ayi~ayi)
ndikuvutika ndikuzuzika inu mulipo
[verse 2]
chumachi ndi changa
magalimotowa ndianga
mumapangira miyala yanga
mafuta ndi anga
ngakhare magetsi ndi anga
zimapangidwa ndimadzi anga
koma nokha nokha mukudzilengela matenda
machilitso ndik~magulitsana
ndinu akhwidzi
muli ndizisisi, sisi, sisi, sisi, sisi, sisi, sih
muli ndizisisi, sisi, sisi, sisi, sisi, sisi, sih
amangolira
[chorus]
amangolira (mayi malawi)
walira (mayi malawi)
amangorila (mayi malawi)
walira (mayi malawi)
amangoti (ayi~ayi~ayi~ayi, ayi~ayi~ayi~ayi~ayi)
ana anga inu
ana anga inu
amangoti amangoti (ayi~ayi~ayi~ayi, ayi~ayi~ayi~ayi~ayi)
ndikuvutika ndikuzuzika inu mulipo
[verse 3]
amandiseka azimayi azanga tikak~mana k~magulu
mai malawi mumakhala ngati simunaberekepo inu
amandidabwa azimai azanga tikak~mana k~maguru
mai malawi mumakhala ngati simumamuopa mulungu
komatu ife timakusilirani
muli ndikanyanja kabwino
muli ndimitsinje yabwino
muli ndikanyengo kabwino
muli ndika thaka kabwino
muli ndizinyama zabwino
muli ndimapiri abwino
ana anu ndiopirila bwino
nkona ndikakhala ndimagwada pansi
k~mpembedza namalenga m’mwamba
chonde mbuye dziko musalilange mulange ine monga kholo lawo
oh my god
[outro]
yah~yah, yah
(mayi malawi)
(mayi malawi)
yaachina seven adah
(mayi malawi)
(mayi malawi)
(ayi~ayi~ayi~ayi, ayi~ayi~ayi~ayi~ayi)
(ayi~ayi~ayi~ayi, ayi~ayi~ayi~ayi~ayi)
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu megan brown, ben toth, lindsay mendez - song 3: i need you, sasha
- lirik lagu dylan elliott - too late to stop
- lirik lagu straightdrop - track hawk
- lirik lagu bleauisnotcool - s.o.s
- lirik lagu saydexxx - и это проблема? (is that a problem?)
- lirik lagu blairose - tell me it's fate (outro)
- lirik lagu dan andriano & the bygones - narcissus, amateur classic narcissist
- lirik lagu cindy 2002 - un homme qui passe
- lirik lagu the federales - dead gulch dan
- lirik lagu beyazıt öztürk - yüksek yüksek tepelere