lirik lagu sagres 014 - time lost
lyrics of time lost by sagres 014
intro
igwiritsitse nthawi aise osapupuluma
no pressure slow but sure aise osapanga phuma
verse
samalira nthawi yakoo kuopa kusekedwa ndi anzako
gwiritsa ntchito mwayi limbikira heavy aise osagwera mphwayi
poti ukayitaya lero uzalira mawa
when you loose your time now you’ll regret pamawa
~n~lipo anzanu ankayiseweretsa
sankamvera makolo zibwana akamawaletsa
pano you better ask me where are they (where are they)
running out up and down day by day (day by day)
anzanu omwe ana pusher pano anavaya ge~colle
zoti last munkachezaa panopa ndi history
achеza nanu bwanji yet you have nothing to tell him
timwеtseni umodzi that’s all you can tell him
that’s y amakuthawana coz nthawi ndi ndlama
they have no time to waste yawo ndiyopanga ndlama
chorus
time lost never gained
when you loose it you’ll not regain it
please guys k~masamala
you better think twice first osangokhala aaa
time lost never gained
when you loose it you’ll not regain it
please guys k~masamala
you better think twice first osangokhala aaa
time lost never gained(gained)
when you loose it you’ll not regain it (gained)
please guys k~masamala
you better think twice first osangokhala aaa
verse
time lost never gained
watengeka ndi anzako oti chilichonse kwao anawapangilaa
za geri mmutumu mulibemo
ukhalira bhawa akazi ndi chamba nk~mati ndi udolo
moti upange za tsogolo
ikakhala fees pano umadyera wayiawala kh0m~ lomwe uchokera
makolo kukulangiza iwe onsamvera
nthawi uononga pano uzayilira pano moyo ukuphweka onse ali moyo
kholo limodzi likadzapita
ndipomwe uzadziwe moyo ndiwovuta
kupanda kusintha nkulingalira uzama uzanong’oneza nazo bondoo
bondoo ooowo
time lost never gained
when you loose it you’ll not regain it
please guys k~masamala
you better think twice first osangokhala aaa
time lost never gained
when you loose it you’ll not regain it
please guys k~masamala
you better think twice first osangokhala aaa
time lost never gained(gained)
when you loose it you’ll not regain it (gained)
please guys k~masamala
you better think twice first osangokhala aaa
hook
you better think twice first osangokhala aaa
hook
you better think twice first osangokhala aaa
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu joshua brew - you make me want to break things
- lirik lagu xxxtraktor - banská bystrica (feat. adam skot)
- lirik lagu enygma rapper - procurar e destruir (remake)
- lirik lagu hinterlandgang - der himmel kann warten
- lirik lagu chilli vanilli 2 - wahrheit (pastiche/remix/mashup)
- lirik lagu black dresses - wounded animal
- lirik lagu the security breach show - find myself again
- lirik lagu nexz - starlight
- lirik lagu the_s7venteen - toxic love
- lirik lagu кровь из носа (krov’ iz nosa) & ayomarkiz - no dopamine