![lirik.web.id](https://lirik.web.id/tema/logo.png)
lirik lagu sagres 014 - awida
#intro [joskido]
dzina langa ndine bunda kulanga ana chipwete chalunda
kugawa chibhalo zibhalo year0 k~musiya paukapolo
kanyokhe kanyokhe komabe end ndidzakuyenda
simud~nkula afana mukule kaye mukali khanda chuh
#hook [sagres 014]
ndisanabwere pa bunda, nd~nkati ndidzayiphulah
mix pa den ka eight points nde nd~nkati ndidzad~nkulah
pano ma results now out portal ndukanika kutsekula
year0 ayinga apa zavuta apa nde mutu wakula
ndisanabwere pa bunda, nd~nkati ndidzayiphulah
mix pa den ka eight points nde nd~nkati ndidzad~nkulah
pano ma results now out portal ndukanika kutsekula
year0 ayinga apa zavuta apa nde mutu wakula
#verse 1 [sagres 014]
nditangobwera k~mene ndima leader life ya hiphop
mfana wa ding mfana wa llz wosemphsna nditi zikwapu
year0 ayinga apa zavuta apa nde mutu wakula
mid am on zеro end i don’t know apa asabula
mix chimfana cha llz nd~nkangodzimva u bnd
kudzuka mammawa kuvaya pa commoz pena kugona ku gmt
#cont….[temano]
yama badman eeh, portal kuopsa ngati ndе ndiku vatican eeh
acting very bad pa bunda ndine veteran, shaa!!!
mutu wakula kugoba frus but still on a front line yeah
feeling vibes mix nde timango dripper aise
anyani anyani nkati bola mpeze pap
reaching my goals
#hook [sagres 014]
ndisanabwere pa bunda, nd~nkati ndidzayiphulah
mix pa den ka eight points nde nd~nkati ndidzad~nkulah
pano ma results now out portal ndukanika kutsekula
year0 ayinga apa zavuta apa nde mutu wakula
ndisanabwere pa bunda, nd~nkati ndidzayiphulah
mix pa den ka eight points nde nd~nkati ndidzad~nkulah
pano ma results now out portal ndukanika kutsekula
year0 ayinga apa zavuta apa nde mutu wakula
#outro
awida
awida
awida, onse achina ida awida
onse omwa ma ryder ma cider awida
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu naibafva - finalclash - monster (acoustic cover)
- lirik lagu museli mulaima - i'll never be in love again
- lirik lagu garavi sokak - svako ima nekog koga više nema
- lirik lagu tuv - bunny pt. 2
- lirik lagu crumb - side by side
- lirik lagu olivia lyon - cindy lou's revenge
- lirik lagu resse raway - boom
- lirik lagu catana - dime
- lirik lagu cruzando el charco - sin final
- lirik lagu flanders & swann - a happy song