
lirik lagu sagres 014 & lucelba - about time
#verse (sagres 014)
it’s all about the time yoo
kuti zanga zitheke
kuti zanga zitheke kugwa nkudzuka tiyende
inde moyo ndikamodzi koma sufunika phuma
utha kudabwa usanatope kuzangofikila kupuma
sunganjoye usanakule dekha kaye mphw~nga
awa ndimalangizo ndiye tchela khutu nzanga
awo ankanjoya life ali ku secondary
they wouldn’t share with us zomwe amaphaka mumbale
chilichonse ndi nthawi konza kaye tsogolo
zakale zapita maso aone kutsogolo
don’t be taken up with gees oti sangakuthandize
olo utasowa ya bola mogo sangakubandise
you gat to stay focused ona kaye chimodzi
you need to have a circle oyenda nawo limodzi
it’s gonna be alright chabe ungodikila nthawi
have patience and the hope breda osagwera mphwayi
#chorus (sagres 014)
whatever you wanna do
you wanna enjoy life
you wanna live you wanna say you want good life
it’s all about
time! time! time! time! time!
whatever you wanna do
you wanna enjoy life
you gat to wait matter of time
you’ll lead a good life
things gonna be
alright! right! right! right! right!
#verse (lucelba)
kamoyo kaseko life yozungulila, timenyeko 2 pa mwina mutu kubulungila tisipeko bawa moyo ndikupitilila it’s all about time yanga ikudikilila… pakona yangokhala phe phe katsonyo kanuko kw~nga zidzakhala fwefwe zikuduma osati zunuzonso zikunena etse timachenji tanuto ndiye munditukwanitse?… salakwitsa ndinayiwala koma mundimwetseletu turn yanga mmawa … pano mukunditukwana osasamala kankamwa ndithawi yanu big yanga ikubwela mmawa.. ifeyo tinakagoba chonchi idzakwana nthawi kuwala kuposa tochi… kunyozedwa kusalidwa zonse zili m’ buku koma udzasiye phazi amenewo mawu akulu
#chorus (sagres 014)
whatever you wanna do
you wanna enjoy life
you wanna live you wanna say you want good life
it’s all about
time! time! time! time! time!
whatever you wanna do
you wanna enjoy life
you gat to wait matter of time
you’ll lead a good life
things gonna be
alright! right! right! right! right!
eee tangodekha, sulipo wekha
you gat to wait kuti ngini ikhale better
it’s all about
time! time! time! time! time!
eee tangodekha, sulipo wekha
you gat to wait kuti ngini ikhale better
it’s all about
alright! right! right! right! right!
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu nocturnal depression - perpétuelle eclipse
- lirik lagu goees - я ненавижу тебя
- lirik lagu mgk - sad again
- lirik lagu youngfolk10k - cancer moon ( gimme a hug )
- lirik lagu naufal manaf - suicide with princess
- lirik lagu prohlada - вера (faith)
- lirik lagu robert schumann - es treibt mich hin
- lirik lagu social station - into the hold
- lirik lagu luis emilio batallán gonzález - quen poidera namorala
- lirik lagu miki jevremović - sama