
lirik lagu sagonjah & tadala - zima
[chorus]
ndimakukonda
kukhala ngati kukulondalonda
sinkayika koma ndimawopa
wina azachuluka nzeru uzaf~~ka
nkona
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati
[verse 1: tadala]
sindikayika
kuli mtima wako sikutalika
minga yachikondi mayo mtimawu wabayika
nde umaona ngati ndimakusata mapazi
ndikadekha ndekha jenkha manyazi
phone sumandiyankha ndimafoka
ndimafuna pena k~mandikankha
umatalikira
umatayilira
olo namondwe panyanja amakalipira
umandipilira
kupangitsa zinthuzi k~mapitilira
vundula madzi akhoza k~madikira
ndiwe w~nga komabe mtimawu umakusilira
madzi ak~mwa osamapisilira
sanje azikhala nayo mulungu ine ndi nda?
mwina ndikufunika uphungu nde tita?
sanje azikhala nayo mulungu ine ndi nda?
mwina ndikufunika uphungu nde tita?
[chorus]
ndimakukonda
kukhala ngati kukulondalonda
sinkayika koma ndimawopa
wina azachuluka nzeru uzaf~~ka
nkona
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati
[verse 2: sagonjah]
mwina ndi mantha chabe
simmawupeza ndisaname
mwina m’mangawa simnachile ndimilandu yatizibwezi takale
mwina ndi mamuna wansanje
mwina, mwina ndi trauma
chikondi chandiwonetsa zowawa
pano [?] kuteteza mtima w~nga
koma mai mai kalanga
muzitaye zonse ine mmapanga
siine m’ngelo pena ukali
kaduka kuswaya chikondi kutali
koma ngati tingak~mane pakati
tonse tikubwеla kuk~mana mkati
zomwe ndipeleka ndi zomwе ndiyembekeza
[chorus]
ndimakukonda
kukhala ngati kukulondalonda
sinkayika koma ndimawopa
wina azachuluka nzeru uzaf~~ka
nkona
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
[bridge]
zimakhala ngati
zimakhala ngati
nsanje
zimakhala ngati
zimakhala ngati
nsanje
zimakhala ngati
zimakhala ngati
nsanje
zimakhala ngati
zimakhala ngati
nsanje
[chorus]
ndimakukonda
kukhala ngati kukulondalonda
sinkayika koma ndimawopa
wina azachuluka nzeru uzaf~~ka
nkona
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
zimakhala ngati nsanje
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu jeune morty - teen titans go
- lirik lagu kira percocet - умирать вместе (die together)
- lirik lagu great gaia - eternity's end
- lirik lagu dayzemusic - push or shove
- lirik lagu sól fuller - lover girl
- lirik lagu glacier - refresh
- lirik lagu yasmi - киану (keanu)
- lirik lagu boombassador - i found my friends
- lirik lagu ethxrxxl - get geeked
- lirik lagu arcadium (band) - it takes a woman