lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu sagonjah & tadala - wakutowa

Loading...

[verse 1: tadala]
chiphadzuwa, ndangoganiza zokulembera chibaluwa
umve zamumtima kudzera mu mawuwa
love yeniyeni osamasungunula
mwana kuwala kupoiritsa medulla
galu k~mpasa mafupa suzamumva kukuwa
one, two, one, two, mpakana kuguwa
fumbi ndiwe mwini sinzaopa kutuwa
kuonjezera moto sinzalola kufuwa
chilichonse paiwe kusitika
kucho apo naiwe ndikutsilika
chimwali chimfilika
chimwali chofilika
chothobwanyika nde sindingamakhale mofinyika
nd~nkani, ndimayenda mothimbwizika
love sumandipatsa yosisitika
pena nkhawa mayi ndinu osililika
pena nkhawa mayi ndinu osililika

[chorus]
mmeme ndakuwona
ndiwe wakutowa
nane nifuna nilaweko
kuchoka mu m’dima ndiwaleko
nkhawa zanga ndiiwaleko
mmeme ndakuwona
ndiwe wakutowa
mami nifuna nilaweko
kuchoka mu m’diwe ndiwaleko
nkhawa zanga ndiiwaleko
[verse 2: sagonjah]
maso akuwala ukasekelela
mtendere w~nga, nkhopе paphewa
ndithyolera khosi, polimba mkufewa
basi ndiitana nkozi kwanu akadya dеya
ndimakukonda, ndi iweyo ndimakondwa
sindimazionaso ndi munthu wina
zomwe ndimaona ndiwe bae tikuvina
chonchi, chonchi
nde ndaganiza zoti
tikhale pachikondi choti
tikondane, mpaka kudothi
bondo ndagwetsa tingomanga umodzi
bondo ndagwetsa, bondo ndagwetsa
?
sindikupanga za bowa bw~nga
ndingasudeyi, ndingasudeyi
lunsa loyera tavasha

[chorus]


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...