lirik lagu sagonjah & tadala - stupa
(katelo)
k~madekha!!!
life pena imavuta penanso zinthu zimatheka
sadalira utangokhala so you better go relax, work hard
kudzuka m’bandakucha udzakhala khumutcha dont play hard
see dont play hard
see dont play hard
(tadala)
mfana kuthamangathamanga koma sindikuthawa
ngini sikuyenda kukhalira kukwawa
ngati sunamve kuwawa
sungandiuze nthawi yanga izakwana mawa
ngini sikuyenda kukhalira kukwawa
mfana thamanga thamanga koma sindikuthawa
salary yanga ena akushophela bhawa
nde nd~nka ndisaka zitsime zosaphwa
k~mba ndi manja kuk~mba ndimakasu osathwa
ena kusewela ndi moyo ena pompo nathatha
ndi imfa, ndi madzi nthenda zanji zosatha
umphawi kundikundikila toto ndalema
ili ndi thupi langa nawu mkate ndatema
usandifake mawu mkamwa chonde ndakana
tilibe zoziyeneleza panga matama
nde usaiwalire usanandiwalire
allah wata allah ndi ekha ndingamuswalile
ndikupanga zanga mukubwela zanga ndikuphanga
oyenda ndi mpeni, ndi lako lizakupha lupanga
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu money man - ring
- lirik lagu jordylongsocks - dj terrocal
- lirik lagu glacier (oh) - safe in sound
- lirik lagu tezvix - again and again ( ft. dirty whispers)
- lirik lagu brandon mendoza-meza - the stars are my only friends
- lirik lagu hoyofair & ウォルピス社 (wolpis carter) - 口約束 (kuchiyakusoku)
- lirik lagu teccmeta - john wick
- lirik lagu sullynumber1 - dupla doza
- lirik lagu moon goon - voodoo you think you are?
- lirik lagu something to do - water & air