
lirik lagu sagonjah & tadala - simungandisinthe
[verse 1: sagonjah]
sindimayenda ndi mphepo
ndisintha masamba ndi nyengo
tili mokudya misisi ya mtengo
pamene anayambira [?] kasupepo
sindimasintha ndimangoyenda mwina
kusiyana kuganiza basi kuchimwa
sindingasangalatse wina aliyense
kupembeza milungu iwiri sizingatheke
sindingapange zofuna anthu ayi
kusangalatsa gulu mk~malilaso mkati
womanga pagulu k~mbali mvundulamadzi
wandale kusintha msalu uhule wazipani
sindingaiwale komwe ndimachokera
kuzikana ndikusochera
mission ndi yomwe ija
si 2020 koma vision ndi yomwe ija
[chorus]
[verse 2: tadala]
simungandisinthe ndine tadala ndipo ndizakhala
wakhungu lofewa koma mtima wokhakhala
ena amadabwa ndimaw~nga anga
osayankhulisa winatu ndi ma lupanga
umve nkhutuk~mve
ndine mfana wa smart mwaumve
nde sungandiwelenge saona wakuyeriko
man’gombe pamaso mabodza kuseriko
zotere tin~z~ona kale
chilipo chinamufuna m’bale
izi mkambе
sindingakhale nanzikambe
omangosintha uko ukusintha
lero jеzebel mawa nyenyezi titha
simungandisinthe ngati nyengo
sichilichonse chili mdi mtengo
moyo sungagule
mizu yakuya sungazule
olo atatchena ndi gule
ntunda ng’azi mmadzi ng’ona
mbewa yasowa khoswe nona
[chorus]
[verse 3: sagonjah & tadala ]
siingandisinthe ndi ndalama
abwenzi ena umawaziwa akapata
nthawi zina kuli bwino kufa ndi njala
kusiyana mkudyesedwa zopita ku ntaya
sindi~ngadzigulitse ukulu
sinsima yokha, ufulu
simtima okha, uzimu koma chilichonse chabwino ndi mulungu
sungandiuze choti ndikhale
sungandiuze makaka oti ndivale
wakutsina khutu osati wakuweluza ndi m’bale
chikondi pamtendere dikira udwale
zofunika kulimba mtima ngati kadwale
adikira upale
unyike ngati mphale
sakondwa uwale
ife nthiti gwa bola kwao an~n~le
mukawaona otere ananu musamale
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu yangspen - sephiroth
- lirik lagu bnkt:d, noven & lolettin - sohaorszag_v2.als
- lirik lagu faro (ita) - dan dan remix
- lirik lagu rondodasosa - occhi tristi
- lirik lagu braxton hicks uk - bruises
- lirik lagu calboy - cry bout that
- lirik lagu kittenfrontuto - dont mess with us
- lirik lagu jonathan beauchamp - what now?
- lirik lagu illusive anoo - u pala
- lirik lagu lady wray - i ain't ready