lirik lagu sagonjah & tadala - pamene
[chorus: flo mega]
pamene lipenga lidzalilanso
ndipamene nsonzi sindizalilanso
pamene tizamuona ndi maso
dzachoka mumdimaso
[verse 1: sagonjah]
[chorus: flo mega]
pamene lipenga lidzalilanso
ndipamene nsonzi sindizalilanso
pamene tizamuona ndi maso
dzachoka mumdimaso
[verse 2: tadala]
nena ngamo osaopa
pena umafika potopa
nsima akudyesa yolopa
mpachike pa gologota
ulendo waku kenani sitinafike quarter
kufela mbendera bwana sindikufela nyota
sizifunika phuma, m’memo wa gulu pansi
suzandiona pa kh0m~ pako ndadula phazi
ulibe nthumazi manyazi
nkhondo ndi anasi
ngati sakukhesa mwazi monse akusiya nyasi
[verse 3: sagonjah]
[chorus: flo mega]
pamene lipenga lidzalilanso
ndipamene nsonzi sindizalilanso
pamene tizamuona ndi maso
dzachoka mumdimaso
[verse 4: tadala]
osamatha mawu pama kampeni
tili tonse bwanji ukundisungila ka mpeni
ndikalowa m’boma zanga ndipakule
chikwama cha mloma or mphasa ndiyalule
ntchito k~malembana akubanja
muzilimbikila k~matiuza akunjanja
sitingaiwale wa nzeru asunga mawu
samakhazikika okudya thako lagalu
tadya nawo usipa matemba dzana lija
likulemba lokha pa khoma dzanja lija
ngati sakuwona muphamike mate mmaso
sodom ndi gomorrah owelenga khala maso
tawonana maw~nga,mw~ngokoma pakamwa
zonse sungaphangile tawonani mwatsamwa
nde pano tadziwana
chinamfuna m’bale chilipo
m’bale ife tidakalipo
[chorus: flo mega]
pamene lipenga lidzalilanso
ndipamene nsonzi sindizalilanso
pamene tizamuona ndi maso
dzachoka mumdimaso
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu kamixxbleach - swervin
- lirik lagu layla rhule - the boom boom
- lirik lagu деси слава (desi slava) - хиляди неща (hilyadi neshta)
- lirik lagu darvishi - him
- lirik lagu butrint imeri & era istrefi - lonely
- lirik lagu slow j - fogo
- lirik lagu ximbinha & banda - 1+1
- lirik lagu daniel boudzali - honey
- lirik lagu stelios rokkos - thalassa
- lirik lagu abg rocky - until