lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu sagonjah & tadala - amayi

Loading...

[verse 1: tadala]
yo check it
moyo umakoma ndi inu pambali
mumandiuza zonse ndi nthawi sunga sabali
keep your ears on the ground maso penya patali
mukayankhula i have to listen makani kw~ngali
ndine dolo ndimadziwa
moyo ndi madziwa
samala masewela samachitila pa diwa
khala olimbikila muli m’nyozo mu usiwa
chisoni mk~matenda kuli zinkhani kusiwa
dziwa adzakuiwala palibe chamuyaya
dziwa ndi ife tadala kuli konse ukukhala
khala chitsanzo, nthanga mu chipatso
osaiwala k~mapemphela moyo ndi mphatso
palibe chingakulake
ndiwe chimfana cha lucky
nzeru za mwana zagona pakulemekeza make
ndi atate
siya phazi
osakheza mwazi
maso m’maso mwa munthu osayang’ana pansi

[chorus: quest]
amayi anati
ine ndapita
anthuwa ndi nkhondo
samayamika
amayi anati
ine ndapita
chikondi pa dziko
cha balalika
amayi anati
ine ndapita
anthuwa ndi nkhondo
samayamika
amayi anati
ine ndapita
onani zi nkhondo
zalakatika
[verse 2: sagonjah]
moyo umakoma ndi inu pambali
mumandiuza zonse nthawi sunga sabali
lero munapita kunapita wambali
k~midima koma mu mtima mw~nga ndinube nyali
wali wali kuyenda chisogolo nkhope osepenya pansi
simunalele chitsilu munabeleke nsillikali
zina ngati nkhaza koma munawonеtsetsa
nkhondo yo ikamabwela nzakhale okonzеka
unyule uphule nsanga uzawaziwe abale
ndi amalume anampeleka matafale
chokuya umadziwa chikaphwa
maluwa sungawunukhize uli manda
anthu sachedwa kuyiwala
kuwelenga zikw~ngwani, uh ndi misala
uzipanga zinthu mma chete
chomwe sakudziwa sangachilepheletse

[chorus: quest]
amayi anati
ine ndapita
anthuwa ndi nkhondo
samayamika
amayi anati
ine ndapita
chikondi pa dziko
cha balalika
amayi anati
ine ndapita
anthuwa ndi nkhondo
samayamika
amayi anati
ine ndapita
onani zi nkhondo
zalakatika
[chorus: quest and tadala]
amayi anati
amayi anati
anthuwa ndi nkhondo
anthuwa ndi nkhondo
samayamika (samaya) samayamika
(samaya) samayamika (samaya)
ona zi nkhondo
zalakatika aaah


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...