lirik lagu ritaa - mubwere
ritaa mubwere lyrics
oh, sispence, oh oh oh
ritaa.. h~llo?
(verse 1)
munachoka kuti mukukasaka ndalama
mpaka lero simunabwelerenso
munachoka kutisiya ndi amai athu
koma simunabwelere..
simumatumizanso chithandizo kunyumba
koma zoti mukuchita bwino tik~mva
sitimadziwa ngati mumatiganizira
sitimadziwa ngati mumatik~mbukira
(chorus)
mubwere kunyumba
mubwelere kunyumba
mubwere kunyumba
mubwelere kunyumba..
(verse 2)
tinakula, otilera ~n~li mai athu
kuvutika pamodzi ndi amai athu
komanso mutangopita
achimwene anatisiya
ana anu akungolira
chilichonse kuvutikira
phone yokha mukanatiimbira (h~llo?)
kalata yokha mukanatilembera (you know)
sitimadziwa ngati mumatiganizira
sitimadziwa ngati mumatik~mbukira
(chorus)
mubwere kunyumba
mubwelere kunyumba
mubwere kunyumba
mubwelere kunyumba
(bridge)
ohh, mubwelere kunyumba
oh, oh , oh ..
mubwelere kunyumba
(chorus)
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu maluke cefa - juice
- lirik lagu valete - mulheres da minha vida
- lirik lagu lilmaziijugg - internal rage
- lirik lagu no expectations - energy (feat. lucky & deuce)
- lirik lagu normunds rutulis - es gribu tā
- lirik lagu raresoulgod - digitaldream
- lirik lagu altar - tributo al rey (esdras)
- lirik lagu hiddentrapninja - laugh it up
- lirik lagu pink matter - quicksand
- lirik lagu роман бестселлер (roman bestseller) - пой (sing)