lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu praise umali & faith mussa - chimwana changa

Loading...

[intro]
mayo! chalowelera! (chalowelera dele!)
mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera (chalowelera dele!)
mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera! (chalowelera dele!)
mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera (chalowelera dele!)
mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera! (chalowelera dele!)
mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera (chalowelera dele!)

[verse 1: faith mussa]
mwana w~nga ukupita (iwe! iwe, iwe)
chimwemwe ndi chisoni (iwe! iwe, iwe)
zagwira mtima w~ngawu (iwe! iwe, iwe)
times are bad and we know that
pamene ndingoyimba

[chorus: faith mussa]
(mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera!)
iwe k~makapemphera uko (mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera!)
sinkufuna kuzalira mwana w~nga ine (mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera!)
osati chalowelera dele (mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera!)
ndati k~makapemphera uko! (mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera!)
usakalowelere (mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera!)

[verse 2: praise umali]
k~mene ukupita uko (iwe! iwe, iwe)
iwe ukadzasochera ah (iwe! iwe, iwe)
mh mwana w~nga follow the light (iwe! iwe, iwe)
iwe follow the fire
pamene ndikuyimba
[chorus: praise umali]
(mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera!)
mwana w~nga don’t forget to pray (mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera!)
i don’t wanna lose you (mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera!)
iwe udzikapemphera uko, iwe k~makapemphera uko (mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera!)

[outro: faith mussa]
papapa (mayo! chimwana changa dele, mayo! chalowelera!)

iwe k~makapemphera uko
osati chalowelera dele

Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...