lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu ngozi family - atate

Loading...

[verse 1]
popita ku nchito a ibala to siya
ndalama ya chakudya pa nyumba
ngati ba choka ku nchito
ba pitila to bar
balezela moba wa 10 kwacha
pobwela ku nyumba ati iwe mukazi w~nga
nipase vi nsima na vi ndiyo
amai nabo ati imwe mulibe ku siya ndalama ya chakudya pano pa nyumba
atete iwo a yamba to kalipa
avula ma jacket ati nizaku lungiza iwe

[chorus]
a~a~atate lekani k~menyana ndi akazi atu
a~a~atate lekani k~menyana ndi amai atu
a~a~atate lekani k~menyana ndi amai atu

[verse 2]
please atate lekani ku chita ndeu
ine sindifuna ku menya amai anga
popita ku nchita mosaibala ku siya
ndalama ya chakudya pa nyumba
chif~kwa ntau ina ana onse
azankala ndi njala pano pa nyumba
amai nabo akati ayanguleko imwe mwa yamba ku bachita ndeu
[chorus]
a~a~atate lekani k~menyana ndi amai atu
a~a~atate lekani k~menyana ndi amai atu
a~a~atate lekani k~menyana ndi amai atu

[intrumental]

[chorus]
a~a~atate lekani k~menyana ndi amai atu
a~a~atate lekani k~menyana ndi amai atu
a~a~atate lekani k~menyana ndi amai atu


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...