lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu namadingo - pefekiti

Loading...

ndiloleni ndinene zoona zamkaziyu
chili chonse chili muchimake pefekiti
mlingo oyezedwa bwino, thupi logwilana bwino
pachingelezi, kompakiti
ndipo sindi kusamala za mkazi wina kupatula uyu
ena ndikuwathila doom ma insekiti
kandalama komwe ndinapeze, pakutha pa mwezi
tizankala pansi together, k~menya ma bajeti
tikalipila ya nyumba ya rent, kwina ku tik~manga yathu
kukabwela change shopping, ku super maketi
ona zako ndizanga baby, palibe ichi ndichaine ndekha
chili chonse ndi chako, olo yanga waleti, baby uli pefekiti

yemwe amati kulibe pefekiti
akazakuona khope yako, baby
yemwe amati sadaone pefekiti
akazakuona thupi lako, baby
azatula pasi udindo wabungwela impefekiti
kuli kuvomereza kuti kuli ma pefekiti
azatula pasi udindo wabungwe, lopezerana zif~kwa
kuvomereza kuti kuli ma pefekiti

yemwe amati kulibe pefekiti
akazakuona khope yako, baby
yemwe amati kulibe wapefekiti
akazakuona thupi lako, baby
azatula pasi udindo wabungwela impefekiti
kuli kuvomereza kuti kuli ma pefekiti
kuli pefekiti
pefekiti
kuvomereza kuti kuli ma pefekiti
pefekiti

514898 iyi yanga pasiwedi
gwira gwira phone, baby
palibe zopangana cheat
i love you for real, now and forever more
osandikaikira sindine sasipekiti
ona zakale zapita zasala zasopano za awiri. baby
no ma drama, no chipwilikiti
ndipo singalole wina akujaile akuseweresa my first lady
ulemu wako risipekiti
mawa tipite ku mpingo
kaya ku khoti tikasaine marriage certificate
chimodzi modzi katundu ugula mu shop umboni ndi ma lisiti
sizongotengana panjira, opanda protocol (protocol)
ngati malonda ogula kwamavenda muma street
timasuke tipange mwana, azinditchula adadi
umaziwa ka marriage prodakiti
pang’ono ndi pang’ono, baby
sikulina tizakweza range
koma lelo tiza kwera ka sitaleti uli pefekiti

yemwe amati kulibeko pefekiti
akazakuona khope yako, baby
yemwe amati sadaone wapefekiti
akazakuona thupi lako, baby
azatula pasi udindo wabungwela impefekiti
kuli kuvomereza kuti kuli ma pefekiti
azatula pasi u chairman wabungwe, lopezerana zif~kwa
kuvomereza kuti kuli ma pefekiti
uli pefekiti, uli pefekiti
iwe gelo mmm hmm (iwe gelo mmm hmm)
ona tumaso twako (tumaso twako)
tioneka (tioneka)
ngati nyenyezi gelo
yamamawa gelo
timawu twako (timawu twako)
tumaveka ngati angeli, baby
ak~mwamba, baby
koma yemwe amati sadaone pefekiti
azaone khope yako lako, baby
yemwe amati kulibe pefekiti


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...