lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu molto - kale

Loading...

verse 1

makolo aka kamba ayi tinaleka k~mvela

zimene amati’uza tina vala matu mphela

lomba apa kuli big papeh ma blesser ndi ehh ahh

ena akazi aka enda, kunyumba sabwelela

zosaona taziona kale ndisowa nadiso yoti ndi vale
ana akadzi akonda ciphale

decent clothing ivo ndi vakale

umoyo ndiwe wekha tisangale

k~ma matenda alibe cibale

cikanga mowa anzanga asila

ena nimisala bvuto ni mbanje

(chorus)

nyengo ino zosaona taziona kale
anzanga onse gone tina shika kale

lomba kwabwela blesser amamucha dale
ati you only one live once ife tisangalale

nyengo ino zosaona taziona kale
anzanga onse gone tina shika kale

umoyo ndiwe wekha uzisunge mbale

ana a lomba aona mowa ngati ndi ciphale

(chorus)

nyengo ino zosaona taziona kale
anzanga onse gone tina shika kale

lomba kwabwela blesser amamucha dale
ati you only one live once ife tisangalale

nyengo ino zosaona taziona kale
anzanga onse gone tina shika kale

umoyo ndiwe wekha uzisunge mbale

ana a lomba aona mowa ngati ndi ciphale

verse 2:

we saying we god’s vessels but what’s our use if there’s nothing we contain

ndife thupi la mbuye koma conde ndikufunseni
is god really pleased with what we’re doing

what’s the difference between us ndima soldier a caesar ana punda “mpandeni”

can the body achieve its goal if maganizo ndi osiyana

kwendo lili k~m’poto dzanja lifuna k~m’maba

we not moving in one accord mpingo zelakwisana

lomba war is in the church,thupi lagawikana

how will we spread the gospel tidana ndi osabona

ayi osani jaja zimene nikamba nizoona

mahule machakolwa h0m~~s~xuals ndi mbava

cinthu ti iwala n’cimodzi naonso amamva

(chorus)

(nyengo ino zosaona taziona kale
anzanga onse gone tina shika kale

lomba kwabwela blesser amamucha dale
ati you only one live once ife tisangalale

nyengo ino zosaona taziona kale
anzanga onse gone tina shika kale

umoyo ndiwe wekha uzisunge mbale

ana a lomba aona mowa ngati ndi ciphale) x2


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...