lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu mistah yemie - iwe

Loading...

[intro]
yeah yeah eeeh eee eeeh
mmmh mmmh yeah eeeh
a tswai tswai tswaai
yeah yeah eeh eee eeeh

mmm mmmmh
ajawa you already know
yeah yeah
yeah eee eeeeh eeeeyi eeeyi
[verse 1]
ndichikondi chotani chokakamizaaa
yankho lasowa nkama ganizaaa
kapena ndikh0m~ lopapatizaaa
yeah eeee iyeah eee eeeyi

ndikapandaubwera kwanu ndekuti sinkuona
sitiyankhulana nkapanda kuimba phone
ndikapandaubwera kwanu ndikuti sinku
oooh wou wou mana gyal gyal iwe(iyeah eeh)

[hook]
koma mtima w~ngawu umakondera iwe
m’maganizo mw~nga mumayenda iwe
pena ndimakhara olakwa kamba ka iwe
mavuto onsewa nchif~kwa cha iwe

iwee iwee eeehyi
(ndimakondera iwe)
iwee iwee eeehyi
(ndimafila iwe)
iwee iwee eeehyi
(ndidzafera iwe)
iwee iwee iwe iwe iweeyi
(ndidzamangidwa ine)
[verse 2]
poti awa ndi maso, samaona zamu mtima
nde zimangotheradi mu mtima
nk~maganiza kuti ndingosiya mwina
koma taona m’mangotchula lako dzina

ndayesera kochuluka
nzosathekautuluka
palibe angafike ndiwe wekha uli pachuluka
ena sindiona ine ndangopunduka
taona gyal kwaine ndiwe ofunika

[hook]
koma mtima w~ngawu umakondera iwe
m’maganizo mw~nga mumayenda iwe
pena ndimakhara olakwa kamba ka iwe
mavuto onsewa nchif~kwa cha iwe

iwee iwee eeehyi
(ndimakondera iwe)
iwee iwee eeehyi
(ndimafila iwe)
iwee iwee eeehyi
(ndidzafera iwe)
iwee iwee iwe iwe iweeyi
(ndidzamangidwa ine)
[verse 3]
ndimaziva olakwa ukamaoneka okwiya
ukangokhara duu kundiyankha ukangosiya
mu mtima zimabaya
mutu kukula papaya
nanji chilichose ukamangoyankha kaya

koma gyal iwe fusa feli iwe
zoti m’makukonda he go tell you iwe
mi seh gyal iwe fusa feli iwe
i go die for you he go tell you iwe

[hook]
umakondera iwe
(ndimakondera iwee wee weeyi)
mumayenda iwe
(mumayenda iwe gyal eeeyi)
kamba ka iwe
(kamba ka iwe kamba ka iwe)
nchif~kwa cha iwe
(chif~kwa chaiwe yeah yeahyi eeeyi)

(ndimakondera iwe)
iwee iwee eeehyi
(ndimafila iwe)
iwee iwee eeehyi
(ndidzafera iwe)
iwee iwee iwe iwe iweeyi
(ndidzamangidwa ine)


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...