lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu maskal - ndiwe wanga

Loading...

verse; 1
pazachikondi chako dziwa ine ndi mboni
sindinalakelake kupita ku joni
chikondi cha iwe ndi ine sicham’mafoni
nchif-kwa sindinapite ku bank kukatenga loan
chikondi chathu chobeba chanoninoni
umandizula moyo ukapereka moni
umandik-mbutsa za kwathu k-mangoni
ndakondwa umadziwa kuti ine ndi m’goni

chorus-2
ndiwe w-nga ndiwe kuwala kw-nga
ndiwe w-nga ndiwe nyenyezi yanga
ndiwe w-nga ndiwe w-nga ndiwe wapamtima w-nga
ndiwe w-nga ndiwe w-nga nyenyezi yanga
ndiwe w-nga ndiwe kuwala kw-nga

verse; 2
ndikakha pansi ndimadziwa ndiri ndi mzanga
kuyenda limodzi tifanana maw-nga
amandinena ati ndiri nyanga
asatilongoze monga ichita nkhanga
ndithudi ndilonjeza ndzakutengela kunyanja
nthawi imeneyo tikukonzekera banja
ona ambiri akutiombera m’manja
mpakana wena kutimangira nsanja

(back to chorus)

verse; 3
chikondi chathu chansangala sizachisoni
ena amasangalala akatipatsa moni
unasiya amabenzi onse ndimalinkoni
amat-thila madzi ndik-maimba h-rn
akamadutsa baby, samamvetsa baby
ngati andale baby, ali pa njale baby
zimawawawa baby, kuiwala mawa baby
ngati moyenda baby, ife tikuyenda baby!, hee!

(back to chorus till the end)


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...