lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu mario bro's (mw) - blaze yodella

Loading...

[intro: dirty flo]
nduvaya yeah
nduvaya, nduvaya
yeah nduvaya
ayo billy
yeah

[pre~chorus: dirty flo]
nduvaya ufuna ndizidikira ndani?
tayang’ana mkati uwone ali ndi ine ndani?
oh, oh ufuna kudziwa chani?
tayiponya patali mungofupikitsa nkhani

[chorus: krazie g]
we keep it on fire we blaze yodella
drill on the road whole squad propella
no competition anatitopela
we just pulled up with the whole opera

[verse 1: virus infectious]
one, two imasiyana ndi two, one
nde anthu ena amafuna nzithuwa
ndikuwa ukamva ululu tuluka
fika bulu, potetsa green nduluka
gwetsani kufuntha
ndendende bars ndi ine kethe!
ngati ndinamveka mphete botolo
oh! no! no! botolo verse yolembera kutulo
ndikudyani mpanikizani ndisizani competition, we see none
ndе mvesera pano ndinakwiya (ha)
ukubwera ifе tinapita (ha)
zamasewera ndinasiya (ha)
tikungokwera level ina (ha)
[pre~chorus: dirty flo]
nduvaya ufuna ndizidikira ndani?
tayang’ana mkati uwone ali ndi ine ndani?
oh, oh ufuna kudziwa chani?
tayiponya patali mungofupikitsa nkhani

[chorus: krazie g & dirty flo]
we keep it on fire we blaze yodella
drill on the road whole squad propella
no competition anatitopela (yeah)
we just pulled up with the whole opera (yeah)

[verse 2: dirty flo]
choyamba ndi pembedze yaweh
mfana wovaya ndangoyika jersey ya away
ndiku hitter road koma studio ndi main chick
ndimangoyimba olo usandipatse credit
mwina mumangondiona ngati check up (check up)
utopa ndikudikira sindikudzelako
mark my words ngati mphuzitsi wa grammer
ukafunsa za nyimbo zikuyenda zikubanger
akunama, akunama, ma fans ako samakutsata
indirect otalker indirect
ukufuna kudziwa cha? funsa hillary

[pre~chorus: dirty flo]
nduvaya ufuna ndizidikira ndani?
tayang’ana mkati uwone ali ndi ine ndani?
oh, oh ufuna kudziwa chani?
tayiponya patali mungofupikitsa nkhani
[chorus: krazie g]
we keep it on fire we blaze yodella
drill on the road whole squad propella
no competition anatitopela
we just pulled up with the whole opera

[verse 3: krazie g]
it’s gon’ get cold when i catch you
stoned ndine statue
few shots tryna see what erykha badu
sindichedwa ndi anthu, mwina udikire part two
no enemies, just anime like cartoons
peace signs takwera mwamba kawiri
gang ndiyakatswiri, don’t be nosey ngati siswiri
mind your business why? mantha si awiri
ndikawawa piripiri so many beats silly billy
ndine king, akufuna azindidhuda
malingaliro kusakaniza ndi buddha
ndine spring ngati nzako ukandikhudza
koma sindikungokhala ndingo njanja ndikudutsa

[pre~chorus: dirty flo]
nduvaya ufuna ndizidikira ndani?
tayang’ana mkati uwone ali ndi ine ndani?
oh, oh ufuna kudziwa chani?
tayiponya patali mungofupikitsa nkhani
[chorus: krazie g]
we keep it on fire we blaze yodella
drill on the road whole squad propella
no competition anatitopela
we just pulled up with the whole opera


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...