lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu lil al - maye$o

Loading...

[intro: lil al]
too much
big slizzy, you know what i’m sayin’, lil’ twin?
baxter is too nice
i’m sayin’, lil’ twin, i need to pull up
put the young kids on some game, real talk
huh

[chorus: lil al]
khala chete ndikuwuzire mayeso, shh
khala chete ndikuwuzire mayeso, shh
khala chete ndikuwuzire mayeso, shh
khala chete ndikuwuzire mayeso (khala chete ndikuwuzire mayeso)
uzindipatsa lighter osati machesi (uzindipatsa lighter osati machesi)
uzindipatsa lighter osati machesi

[verse 1: lil al]
ndimakonda kusuta ma cheesaro (cheesaro)
ndimafinyika ndikakhala ndili kubwalo (ndili kubwalo)
bola ndikhale cellular olo ndika bizarre (bizarre)
ngati ukufuna kuyamba kupanga za mizzo ndi zako (ndi zako)
kukuphuzula ungazayese wizzo ndi nzako (ndi nzako)
yeah, tikamatsika pa stage uk~mva kuwawa zidendeni
tinamva kuti munayamba ku marcher mwadya [leaf?] ’bout ten
imakaye ndikuphalire
[chorus: lil al]
khala chete ndikuwuzire mayeso (khala chete ndikuwuzire mayeso)
khala chete ndikuwuzire mayeso (khala chete ndikuwuzire mayeso)
khala chete ndikuwuzire mayeso (khala chete ndikuwuzire mayeso)
khala chete ndikuwuzire mayeso (khala chete ndikuwuzire mayeso)

[interlude: em~el]
what? huh
em~el, em~elizzo, nah mean?
none of you n~ggas f~ckin’ with me, lil’ twin
nah mean?
steppin’ on these n~ggas, twin (steppin’ on them)

[verse 2: em~el]
nthawi zonse ndimakhala ndikuwonweka trill (sh~t)
gangster kwambiri sindingamaposte ma meme (meme, sh~t)
style safe ngati tikurecodela ku mim (mim)
sindikufuna kupanga zibwezi ndikufuna kupanga ma mil (ma mil)
kape sitichedwa k~mutuluka akangopanga zausiru (zausiri)
vuto lake munazolowera kupanga zinthu zapanyero
ikakhala dancehall ndimapusha ndine mwana ma kartel (yeah)
aliyense amadziwa lizzo amakonda ma girl
aliyense amadziwa lizzo amakonda dinero (lizzo)
ma hater onse chaka chino aku mwalira (akudhiwa)

[interlude: em el]
see what i’m sayin’?
all my opps dyin’ tonight, lil’ twin
nah mean?
see i whack on this b~tch, lil’ twin, see i whack, haha, whack
[chorus: lil al]
khala chete ndikuwuzire mayeso (khala chete ndikuwuzire mayeso)
khala chete ndikuwuzire mayeso (khala chete ndikuwuzire mayeso)
khala chete ndikuwuzire mayeso (khala chete ndikuwuzire mayeso)
khala chete ndikuwuzire, ah (khala chete ndikuwuzire mayeso)
uzindipatsa lighter osati machesi (uzindipatsa lighter osati machesi)
uzindipatsa lighter osati machesi (uzindipatsa lighter osati machesi)
khala chete ndikuwuzire mayeso (khala chete ndikuwuzire mayeso)
khala chete ndikuwuzire mayeso

[outro: lil al]
ah, lizzo, wizzo
baxter is too nice

Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...