lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu lil al - kape!

Loading...

[intro]
yo 14 you got another one
ha, hahahaha
lil alzizizo

[chorus]
kape! sangacheze ndine
nchif~kwa zikuyenda ndipo sizingasimphine
sungadizadwe kusiphe, kofwala kuti ndilabwe ndimafunika ndilipidwe
iwe tangowona umene ndayika
tangowona umene ndayika
sungandipose kutchena mukupepuka mafana muk~manyika
huh iwe, iwe tangowona umene ndayika

[verse 1]
belo sh~t ndungoweneka za mtika
ngati ndimamvana ndi rose wabho bho
koma ndi wa cash drip
kungofika pa malo aliyense akufuna andimenyetse sip
tungodripper wa mame sungatipeze tik~menya ma nip
zi ana zuziwa i’m him zungofuna zindidyetse lip
ndungokakisser nipple kenako ndikadye nipla
umaziwa yanga ija sindiphweketsa limbwa

[chorus]
kape! sangacheze ndine
nchif~kwa zikuyenda ndipo sizingasimphine
sungadizadwe kusiphe, kofwala kuti ndilabwe ndimafunika ndilipidwe
iwe tangowona umene ndayika
tangowona umene ndayika
sungandipose kutchena mukupepuka mafana muk~manyika
huh iwe, iwe tangowona umene ndayika
[verse 2]
nda dropper kwambiri ma guy mu game akubanika
ma trapper a ulesi onse nde ndik~maliza
ngati ulibe dollar ndiwe artist wokanika
feature price ndima charger ngati ndikukaniza (yeah, yeah)
anandi b~tcherko kale nde sindimgawatenge serious
kungomubweleka rack munthu wayamba kusanduka mysterious
ha k~machenjera ma kape atha kubela
atandi slima phone ndinawoneka ngati mfana wopepera
but i didn’t care mix ndinali mu club, chi mwana chimandigwedezera
kenako chikundinong’oneza “big slime ndimaku hopera”
ukamuuza boyfriend wanyuowani atakudyera mkaladi

[chorus]
kape! sangacheze ndine
nchif~kwa zikuyenda ndipo sizingasimphine
sungadizadwe kusiphe, kofwala kuti ndilabwe ndimafunika ndilipidwe
iwe tangowona umene ndayika
tangowona umene ndayika
sungandipose kutchena mukupepuka mafana muk~manyika
huh iwe, iwe tangowona umene ndayika

Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...