lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu lil al, em el & 60 grams - umakwana slime

Loading...

[intro: martin meke]
nde pali kagulu aka kodabwitsa
kamatchedwa ma slime, ati ma slime
ahh slime mentality, slime mentality
titanyamula tima cup tawo, ati basi k~matenga codeine kuphatikiza ndi sprite
azimwa azikhala high hmm?
ana opusa kwambiri
nde timakhalatu k~mavala zima trouser zazikulu
kenako k~mazikhwefulaso hmm?
aah!
ayo 1800

[chorus: lil al]
k~mvela nyimbo zanga
umakwana slime, umakwana
top fan ati amangomvera nyimbo zanga
umakwana slime, umakwana
ati zimakape ziku biter ma concept anga
umakwana slime, umakwana

[verse 1: em el]
yeah
diso langa lafira chif~kwa ndimabanda
kamwana kakundi rider ngati yokohama
ana ohitter ife kamapalasa mabwana
mumanama ma guy mumanama
[verse 2: lil al]
ndine dolo ngati madolo ali an zanga (yeah)
ndizitrapabe ndi gang yanga situdana (yeah)
vuto sine ngati gang yanu mulibe shasha
mulowe flee market mukazigulire mpasha (yeah)

[verse 3: em el]
kuposta nditatchena amangoti wow, wow
akuti “come give me d~ck right now, now
yеah, ganja yanga ndiya loud, loud
phone ili pa dnd ndangogweza sound

[verse 4: 60 grams]
street n~gga sindisekеlera zachibwana
ndimakonda zaza, drip ti ana ndi ndalama
kakungondi yan’gana ndakafunsa what’s up?
eko handle sindikupatsa number yapa whatsapp (whatsapp)

[verse 5: lil al]
ayy wasteman sangakhale nzanga wa ine
baddie a delete kaye ig kuti akhale mkazi wa ine
droppin’ every week ndilibe nazo za timing
za hard nthawi zonse ma opps zakudya rock climbin’

[verse 6: em el]
kakufuna chanel, kakuwona ngati mdala wake ndi ineyo
ati mpaka ndizikatengera ku hotel (hotel?)
kakufuna ku breezer ine ndakagulira doppel
ati “em~el will you please be for real?”
[verse 7: 60 grams]
i started trappin’ you boys ain’t for real
standin’ on business forget a deal is a deal
i ain’t stoppin’ till i got a palm jive and that’s good[?]
they be like “where you from” i be like my mothers womb
ma hater ndi sh~t ndimawatampa ku loo
ndima slimer overnight, tapanga set up chi stu

[verse 8: lil al]
yeah
ndakachotsesa nyimbo za aidfest ndi kineo (kineo)
mumanama ma guy, mumanama
faka , lil al, 60 grams ndi achina em el
umakwana slime, umakwana
umakwana slime, umakwana

[chorus: lil al]
umakwana slime, umakwana
umakwana slime, umakwana
umakwana slime, umakwana
umakwana slime, umakwana

[outro: lil al ]
sound god
umakwana
umakwana


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...