lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu lexblez - nduvaya koledzera

Loading...

{hook}
nduvaya koledzera
nduvaya koledzera
nduvaya koledzera oh
nduvaya koledzera (koledzera)
nduvaya koledzera
nduvaya koledzera
nduvaya koledzera oh
nduvaya koledzera (koledzera)

{verse 1}
ndangodzuka ndimatsire
manja muli ka tea eh
ndingomenya nawo squash sindimwanawo madzi eeh
masten ndawauza change sindipeleka olo akanene kwa t.a
ndinangotuluka pa gate
mix ndikwere bus
ndak~mana ndi teoslim
ah ndingoyenda basi
m weezy wandiuza kuti hope gee uku wagula mavelemoti
ndinangoyenda zigzag ndisanamuvelе moti, ndak~mana ndi
gang gang
bligle, silence wе chen zhen
aku dripa za khofitu
mmanja muli ka cofee
ak~menya ma sip zakut atha kukuyika zimakofitu
ndango joyina gang gang
bligle, silence we chen zhen
mkamwa ndimangofira pain guys
mpaka nnaledzera ndi ten venz oh
{hook}
nduvaya koledzera
nduvaya koledzera
nduvaya koledzera oh
nduvaya koledzera (koledzera)
nduvaya koledzera
nduvaya koledzera
nduvaya koledzera oh
nduvaya koledzera (koledzera)

{verse 2}
shakaaa
pamene paja ndinazangogeya
kuzifiratu kuti eyaa!!
k~mangoyenda zig zag ngati nkhuku yachitopa
dusty d wagona (ah) ndimadziwa chitopa
pamene paja axlet kuzangofika (eh) lero nde timwanyikatu
ma bottle kuzangogwa pansi (eh) lero nde tiphwanyikatu
pamene paja maso ali red (ah)
mpaka wina aliredi
ndinangovaya den straight man wapabed
bro yapeza pa den ine nde aah palibedi
mafana kusokosa panja
ndafikatu deni ooh paja
ati lexblez wapenga
ak~mvana ndi mazo openga
daily ak~mangosokosa
ak~mamwa zopenga
inspector wandiwuza
apolisi azakutenga oooh!
{hook}
nduvaya koledzera
nduvaya koledzera
nduvaya koledzera oh
nduvaya koledzera (koledzera)
nduvaya koledzera
nduvaya koledzera
nduvaya koledzera oh
nduvaya koledzera (koledzera)


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...