lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu leslie (mw) - kalilore

Loading...

[intro]
oh, oh
leslie
sispence on the board
(bodza ayi)
(bodza ayi)
(bodza ayi)
(bodza ayi)
(bodza ayi)
(bodza ayi)
(bodza ayi)
(bodza ayi)

[verse 1]
kalilore ndiwuze ndikupelewera pati, oh, oh
see these men running away from me
what do i do now? kalilore iwe

[pre~chorus]
kapena umandinamiza ine, nati ndine okongola ine
ndine olimba mtima ine, koma nono
lero lokha bodza ayi
ak~mandiseka munthune, ak~mundisala munthune
lero lokha bodza ayi
ak~mandiseka munthune, ak~mundisala munthune
[chorus]
bodza ayi
bodza ayi
bodza ayi
bodza ayi
(lero lokha, ayi)
bodza ayi
bodza ayi
bodza ayi
bodza ayi
(lero lokha, ayi)

[verse 2]
ndiye ndiwuze lerori, chikusowa nchani pa ine? pa zonse, zonse
ndizikonze bwanji?
ndivale bwanji?
ndiyende bwanji?
ndiziphodе bwanji?
ndipange bwanji? (ndatopa ine)

[pre~chorus]
kapena umandinamiza inе, nati ndine okongola ine
ndine olimba mtima ine, koma nono
lero lokha bodza ayi
ak~mandiseka munthune, ak~mundisala munthune
lero lokha bodza ayi
ak~mandiseka munthune, ak~mundisala munthune
[chorus]
bodza ayi
bodza ayi
bodza ayi
bodza ayi
(lero lokha, ayi)
bodza ayi
bodza ayi
bodza ayi
bodza ayi
(lero lokha, ayi)

[verse 3]
mirror, mirror on the wall
lie to me no more
i can’t take this no more
ndizitaye, tayimakaye, kukhalira kunamizidwa ndima guy
what a shame, tell me who is to blame?

[outro]
lero lokha bodza ayi
ak~mandiseka munthune, ak~mundisala munthune
lero lokha bodza ayi (lero lokha ayi)
ak~mandiseka munthune, ak~mundisala munthune
lero lokha, ayi
lero lokha, ayi
(sispence on the board)


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...