lirik lagu langwan piksy - tsoka liyenda
k-mbire adanka nawo
palibe akanakhonza
anasiya pa dzuwa anawo
anayesa ndi malodza
ankati satana
wakhala pa nsana
kuyamba kudana
kufuna kuphana
kuthana
nzosauzana
nthawi yakwana
buluzi wa easy chitseko cha mpana
chorus
anapita ndi nyanga zomwe k-manda
anapita ndi nyanga zomwe k-manda
ayo
tsoka liyenda
ayo
tsoka liyenda
bambo awa -n-li chikhwaya
ana moyo wawo sanamve kuwawa
ku school akapita amathawa
zinavuta ndi za nchere -n-lawa
yes
sanauzidwe za moyo
anapeza bwanji makolo
chuma
moyo unakoma
opanda zo khoma
kupeza izo afuna
ohh dzi ana ulesi
bambo awo atsamira nkono
akuti zonsezi
ndi curse
chayabwa chitedze
mavuto pang’ono see they stressed
chorus
anapita ndi nyanga zomwe k-manda
anapita ndi nyanga zomwe k-manda
ayo
tsoka liyenda
ayo
tsoka liyenda
mudziwaphunzitsa ana
skupangira pa mawa
asamayese ngati ophweka moyo
mukadzapita adzakhala akapolo
musama yiwale
kuti zanu munapanga kale
nzeru zanu sizingatsale
mungadzavut-tse abale
mdzakolola zomwe mudzale
chuma ichi sangasamale
ngati panopa simuphunzitsa
mapangidwe ake muk-mpusitsa
tsoka ilo
chorus
anapita ndi nyanga zomwe k-manda
anapita ndi nyanga zomwe k-manda
ayo
tsoka liyenda
ayo
tsoka liyenda
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu kaliraps - fundamentals
- lirik lagu for the fallen dreams - bombay
- lirik lagu fashawn - champion
- lirik lagu for the fallen dreams - dream eater
- lirik lagu mila j - u remind me
- lirik lagu plies - keep pushin
- lirik lagu maximo park - where we're going
- lirik lagu freeway - tolerated
- lirik lagu master p - what the business is
- lirik lagu bryant dope - field of dreams