lirik lagu langwan piksy - kuzizira
kuk-mazizira kukada
tsiku kuchedwa kutha kukacha
tsiku lonse mvula mawawa
sindingachedwe ndidziwe za mawa
mano anga anthu sawaona
sikweni kweni kusekelera
usiku zindivuta kugona
ngati udzudzu ndimachezera
moyo wathu dzana unkakoma
kachikondi kutsekemera
ubwino opanda mwina ‘pena koma
kachikondi kulemelera
chorus
alipo akukukonda?
alipo akukuhoda?
alipo akukugwira?
ndikungoganizira eya
alipo akukuwuza amakukonda kuposa ine? ey
poti dziko langa likuzizira popanda iwe yeah
verse two
chikondi chinali on point
ngati nyimbo yolondola ma note
chinali perfect chinalibe fault
anthu wokamba ankati tiri hot
zoti chikondi chimawawa inali mphekesera
anthu ena akamakamba tinkangomvetsera
anthu akaduka kusowa chotigwetsera
koma lero tandiona ndingo fwenthera
maso anga ayandama in tears
mtima w-nga udzadza ndi fear
usaganize zoti undisiye
ndikungoganizira
chorus
alipo akukukonda?
alipo akukuhoda?
alipo akukugwira?
ndikungoganizira eya
alipo akukuwuza amakukonda kuposa ine? ey
poti dziko langa likuzizira popanda iwe yeah
verse three
kodi chikondi nnakupatsa chija nchokwanira?
kuti udzadikira mpaka nthawi idzakwanira?
ngakhale moto utawotcha udzakakamira?
chikondi chako chikuthawa kodi udzambwandira?
ndiwe wekha ndikufuna mdziko langa dear
mtima wako usakayike ndiwe w-nga dziwa
ndi pemphero langa nthawi zonse uk-mbukira
ndi kwa iwe kokha komwe mtima w-nga ugundira
chorus
alipo akukukonda?
alipo akukuhoda?
alipo akukugwira?
ndikungoganizira eya
alipo akukuwuza amakukonda kuposa ine? ey
poti dziko langa likuzizira popanda iwe yeah
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu maffew ragazino - box office smash
- lirik lagu iamsu - i be on that
- lirik lagu cee lo - only you
- lirik lagu the johan - maaf ku tak memilihmu
- lirik lagu off canal - road to somewhere
- lirik lagu inhollow - our event horizon
- lirik lagu the good mad - sail on
- lirik lagu vonda sheppard - hooked on a feeling
- lirik lagu rounds - falter
- lirik lagu iggy azalea - work