lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu langwan piksy - appettizer

Loading...

chorus
umandipatsa appet-te
ndiwe appetizer
umandipatsa mphamvu zambiri
ndiwe energizer
umanditsitsa mtima
ndiwe stabilizer
umandipatsa appet-te
kantima kofuna kudya

verse 1
chiyambire kukhala nawe ndik-madya zedi
uk-mandipatsa njala ndiwe lucozade
ndukonda kudya nyama wandiyambitsa nkhwiru
chinangwa chokukuta ndicho fruit after meal
and its…kinda strange kudya cha mma seven
eight, nine, ten mpaka cha mma leven
kudya osatopa
dzala ndikutsopa
osanama ngini ili proper
ndeno…ka flavor ka chikondi cha iwe… pine apple
nde… daily chikondi change chingochita pile up
ndi anzanga ndikunenedwa
akuti ndikunenepa
mmene ndudyera zuyenera kukhala choncho k-mene ka
zophika zimamveka zokazinga eti
ngini ili bho yes! i’m lovin’ it
ndikakhala nawe ndiyiwala zambiri
honey tiye tizikhala awiri
chorus
umandipatsa appet-te
ndiwe appetizer
umandipatsa mphamvu zambiri
ndiwe energizer
umanditsitsa mtima
ndiwe stabilizer
umandipatsa appet-te
kantima kofuna kudya

verse 2
sinkuyang’ana za diet ndingodya, mphwa ayi
umachotsa nkhawa zanga zonse ndingomvera ire
ndikondwa uk-mbuka kuti love takes two
chirichonse chingoyenda ambuye mbali yathu
nde…
panopa kudya kw-nga kwafika pa worse
ka soda pambalipa mwina just in case
kuntima kw-ngaku chimwemwe zedi
ndithokoza k-mwamba chif-kwa cha iweyo babe
nkaona nkhope yako k-mva kutsekemera
sumadabwa nthawi zina ndimangosekelera?
mtima wako wokongola ngati umadya make up
nde akuti ndikusiye babe sizithekatu
paja wati ndikuvuta nkudya
usiku cha mma 2 kudzuka nkudya
chikondi chakochi…ngati umathira spice
osanama darling it feels real nice

chorus
umandipatsa appet-te
ndiwe appetizer
umandipatsa mphamvu zambiri
ndiwe energizer
umanditsitsa mtima
ndiwe stabilizer
umandipatsa appet-te
kantima kofuna kudya

verse 3
ndumati nkachoka podya chinan-z-
sindisiya pompo ndidyanso bananas
zafika poti ndayamba k-mana izi
ena ati ndidya mopanda ma manners
kudya osatopa
dzala ndikutsopa
ngati ili subject ndine wosadropa
kudya osatopa
dzala ndikutsopa
osanama ngini ili proper
chorus till fade


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...