lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu kwemogoon - samayankha

Loading...

[intro]
yeah
yahh, ahh
(davinci)
ahh, ahh
yeah

[chorus]
ndikayimba phone imangoti busy
mwina anandiyika blacklist, andiuze
mwina unandiblocker, chif~kwa sumayankha
mwina zinakubhowa zimene ndinapanga
kutumiza ka text, samayankha
olo kuvunga ka vn, samayankha
k~menya video call, samayankha
olo iweyo umu beepe, samayankha, yah

[verse 1]
chama nine, kalowano online
ine pompopompo ‘hie’ , koma no reply men
maybe she got pride or maybe she don’t do love
sikayankha ayi, kaya nchani kamafuna
komabe sindiyiva, inebe ndihalabe
ndizingo beeper olo usandiyankhe
i just want to talk, koma iweyo you don’t want to
umangodusa ngati sumaziwa kwathu
[refrain]
give me a chance, yeah
ndipase mwayi
mwina ndi ineyo amene mangokutayitsa zinthawi
give me a chance, yeah
ndipase mwayi
mwina ndi ineyo amene mangokutayitsa zinthawi

[chorus]
ndikayimba phone imangoti busy
mwina anandiyika blacklist, andiuze
mwina unandiblocker, chif~kwa sumayankha
mwina zinakubhowa zimene ndinapanga
kutumiza ka text, samayankha
olo kuvunga ka vn, samayankha
k~menya video call, samayankha
olo iweyo umu beepe, samayankha

[verse 2]
maybe ’cause i’m broke, koma uziyankhako bho
kuyesa k~menya call, koma you don’t pick up no
koma number yako aise unandipatsa wekha
mwina azinzako anakutalker kuti sindiworker
what’s the problem? tandiuze
mwina vuto ndine, tandiuze
koma dekha, sine opusa
ndangofusa chif~kwa zimandizuza ine
[refrain]
give me a chance, yeah
ndipase mwayi
mwina ndi ineyo amene mangokutayitsa zinthawi
give me a chance, yeah
ndipase mwayi
mwina ndi ineyo amene mangokutayitsa zinthawi

[chorus]
ndikayimba phone imangoti busy
mwina anandiyika blacklist, andiuze
mwina unandiblocker, chif~kwa sumayankha
mwina zinakubhowa zimene ndinapanga
kutumiza ka text, samayankha
olo kuvunga ka vn, samayankha
k~menya video call, samayankha
olo iweyo umu beepe, samayankha

[outro]
(davinci)
samayankha
samayankha
samayankha
samayankha


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...