lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu kiosk mlw - ndiombele m'manja

Loading...

ndimadziwa ndine mfana oopsa
sindimadikila wina andiombe m’manja
(greatness)
ndipanga zanga ndikuchoka ndipo sindimadikila iwe undiombe m’manjaa
(kiooo)

i’ve always been a nikka everybody hates
but blaming me for being myself, that don’t make sense
i tried to tell you nikkas that we ain’t the same
you tryna make this girls to like you
boy i jus make cash
am always in the dojo like a senseii
shawty mad needs time, but i don’t get that
and once you start makin it, the homies get mad
afuna akupondeleze
i don’t stress mayne am proudly a dawg
4:20 then am lighting my blunt
i ain’t a regular kid am from kaliyeka whеre you find less churches and morе liquor stores

ndimadziwa ndine mfana oopsa
sindimadikila wina andiombe m’manja
(somebody clap hands for me)
ndipanga zanga ndikuchoka ndipo sindimadikila iwe undiombe m’manjaa
(somebody clap hands for me)
ndimadziwa ndine mfana oopsa
sindimadikila wina andiombe m’manja
(aahaah)
ndipanga zanga ndikuchoka ndipo sindimadikila iwe undiombe m’manjaa
(somebody clap hands for me)
to my ghetto gees
osadikila munthu achite kukuuza ngini
zoti iwe umatha u should know it from within
nanga bwanji ukugona?
dzuka ukachase_e dream
vuto mukupanga zinthu n’kungofuna kupanga impress anzanu
anthu akakuonani aziti mumatha
adha
izimukuchedwa nazo
big up sangakugulileni olo mandasi
ndikufuna dollar
i don’t need a round of applause
bola ndikupay_edwa olo fans sikujowa
olo kundinena nyimbo zanga sizabho
mangopota zamba nkuiwala kuti kodi ajawa amati chani

ndimadziwa ndine mfana oopsa
sindimadikila wina andiombe m’manja
(somebody clap hands for me)
ndipanga zanga ndikuchoka ndipo sindimadikila iwe undiombe m’manjaa
(somebody clap hands for me)
ndimadziwa ndine mfana oopsa
sindimadikila wina andiombe m’manja
(aaaaahaaa)
ndipanga zanga ndikuchoka ndipo sindimadikila iwe undiombe m’manjaa
(somebody clap hands for me)
the dreams they feel real on rhythm right?
it’s only when you wake up till u realize how things are actually strange


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...