lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu kelvin sings - za iyeyo

Loading...

verse 1

ndak-mana naye
chiphadzuuwa
kukongola kwake ngati ngelo
mayendedwe ake anchiyelo

amapemphela kukada
atseka maso nagwada
baibulo lake k-manja
chimodzi-modzinso kukacha

ati anagwa nchikondi
ndimamuna wantanda
nde ngati ndifuna ndimvane naye
machitidwe anga afane naye

ndimammuna wantanda
mamuna wantandayo
nde ndilekelanji ine oh nana
ndidziwe zambiri

hook

zaiyeyo x3
zaiyeyo

verse 2

nde ndayamba ulendo
oyenda ndintima ahh
cholinga changa nchoti ndikafike
kuli yankho langa

alaliki aineyo
adandifotokozela
zamwana wamlunguyo
ndinso malemba ndikawelenga

ukulu wake undiphunzisa kuzichepesa ine
pakuti njira yopita kwao ndiyopapatiza iye

ndeno ayesu anasamba pati
wandisiya pakamwa kakasi
ndifunisisa nkhale naye phati phati
ine ndiziwe zambiri

hook

zaiyeyo x3
zaiyeyo

bridge

nde ayesu anasamba pati
wandisiya pakamwa kakasi
ndifunisisa nkhale naye phati
ine ndiziwe zambiri

hook

zaiyeyo x3
zaiyeyo


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...