 
lirik lagu kelvin sings - be praised
[intro]
iwe, inva
iwe, inva
iwe, inva
[verse 1]
mumatenga zosweka, ndikuzikongoletsa
mwaitana osachera ndikuwalondera, yaweh
so let my everything follow yaweh
[pre~chorus]
ine sindingalore, kuti nsembe yanu ingopita pachabe
sindingalore, kuti nsembe yanuyo ingolowa m’madzi
nde ndi moyo w~ngawu, ndi luso langali
ndi zochepa zangazi, oh i give it to you, yaweh
[chorus]
be prasied (ndi moyo w~ngawu)
be praised (ndi zochepa zangazi) (oh)
inu mutamandike
mutamndike (oh)
be prasied (ndi moyo w~ngawu)
be praised (ndi zochepa zangazi) (oh)
inu mutamandike
mutamndike (oh)
[verse 2]
for everything you mean to mе, yeah
so lord you deservе all my prasies
you’ve been good to me, yeah
so lord i’ll exort you over all
misomali itatu ndikupulumutsa moyo w~ngawu
nde palibe chuma ndingapeleke kuposa moyo w~nga
[pre~chorus]
ine sindingalore, kuti nsembe yanuyo ingopita pachabe
sindingalore, kuti nsembe yanuyo ingolowa m’madzi
[chorus]
be prasied (ndi moyo w~ngawu)
be praised (ndi zochepa zangazi) (oh)
inu mutamandike
mutamndike (oh)
be prasied (ndi moyo w~ngawu)
be praised (ndi zochepa zangazi) (oh)
inu mutamandike
mutamndike (oh)
[outro]
mutamndike (oh)
tamandike (oh)
oh, oh yeah
mutamndike (oh)
tamwndike (oh)
(ndi moyo w~ngawu)
(ndi zochepa zangazi)
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu playboy simi - billingski
- lirik lagu novela (bih) - čini mi se, čini
- lirik lagu outroeu - tão perto
- lirik lagu josh lumsden - alright! ok!
- lirik lagu confine - scenate
- lirik lagu evilfan - порнозвезда (pornstar)
- lirik lagu #15 (onefive) & #onefive sq - outside
- lirik lagu stupidaxou - курaж
- lirik lagu steiner & madlaina - du kannst nicht gut allein sein
- lirik lagu loric - call me baby