lirik lagu kelvin sings (mw) - mamuna amene ndili
[verse 1]
unandipeza ndili lova, ndilibe kali konse
matumba mw~nga mobowoka, nyumba yopanda khonde
ndekuti dzuwa likawomba, katuk~ma k~maonda
iweyo utandiona, simvetsa chomwe unakonda
utabwera unadilimbikitsa nati ndisabwelere m’mbuyo
chomwe chinali chako naneso ndichanga kuti ndisamasowe tulo
[pre~chorus]
you must be insane to something
how could you give it all in thats nothing in return now, yah
[chorus]
ndikusowa chonena ine (malangizo ako)
andifikitsa pena ine (poti ndine wako)
bwera umunyadire mamuna amene ndili kamba ka iwe
bwera umunyadire mamuna amene ndili kamba ka iweyo
[verse 2]
for i was able enough, yeah
i had room for you my love
ndizizwa ndichisankho chako (chokhala nane ‘khale mnyumba mw~nga mpando munalibe)
pomwe sizinkandiyendera, unagwada ndikupemphera
pamene mwayi unatetera, unandiuza ndimuk~mbuke namalenga
ndikamabwera kuwulenje m’malo mwa nyama ndi denje
k~mandilandilabe ndi chimwemwe, ine pakamwa kakasi
you know pena nkati ndidye flas
most of my days i minded the weather
but i believe god gave you to me to help me keep it together
[pre~chorus]
you must be insane to something
how could you give it all in thats nothing in return, now, yah
[chorus]
ndikusowa chonena ine (malangizo ako)
andifikitsa pena ine (poti ndine wako)
bwera umunyadire mamuna amene ndili kamba ka iwe
(sinditha k~mvetsetsa)
(nkhawa zonse unathetsa)
bwera umunyadire mamuna amene ndili kamba ka iweyo
(sinditha k~mvetsetsa)
(sim’mamvetsa mammie, k~mvetsa mommie)
bwera umunyadire mamuna amene ndili kamba ka iwe
(sindikanakwanitsa ndekha, ndeka)
bwera umunyadire mamuna amene ndili kamba ka iweyo
([?])
[outro]
ndikusowa chonena ine
malangizo ako, andifikitsa pena ine
poti ndine wako
bwera umunyadire mamuna amene ndili kamba ka iwe
bwera umunyadire mamuna amene ndili kamba ka iweyo
eh, yeah
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu dj kas - party like a freak
- lirik lagu deathless legacy - circus of the freaks
- lirik lagu hellscene - u already know
- lirik lagu deathpop - punk
- lirik lagu meladettask - five six seven eight
- lirik lagu djinee - ego
- lirik lagu matthew moore - savannah
- lirik lagu watchhouse - new star
- lirik lagu zarleo - state of mentality
- lirik lagu lacuna777 - murda talk