lirik lagu kelvin sings (mw) - kuyambila lero
[verse 1]
ndinafatsa kulingalira ine, baby
nkhawa inandigwira ine, ine, ah
mandalitso onsewa dziwa amasawutsa mtima w~nga
komwe kuli kokuya sikomwe ndinaponya mbedza yanga
[pre~chorus]
koma ndazindikira kuti kunja konseku palibe amene angandikonde ngati iwe
kundivetsa ngati iwe
nkona ndidza kwa iwe
[chorus]
chikondichi ndi chako, chako, chako
mtimawu ndi wako, wako, wako
udziwe kuyambila lero, yeah
udziwe kuyambila lero, yeah
zonsezi ndi zako, zako, zako
mtimawu ndi wako, wako, wako
ukamagona usiku wa lero, yeah
udziwe kuyambila lero
[verse 2]
eko mtima w~nga utenge
palibe amene angawusamale bwino
chauta nkhawa zathu ansenze
palibe wina angazichengete bwino
nde kuli konse tikafika (kafika)
nyengo zathu zizasintha (zasintha)
koma ndiyambe nkupepesa
(pepa darlie ndinaswa mtima wako)
[pre~chorus]
koma ndazindikira kuti kunja konseku kulibe amene angandikonde ngati iwe
kundivetsa ngati iwe
nkona ndidza kwa iwe
[chorus]
chikondichi ndi chako, chako, chako
mtimawu ndi wako, wako, wako
udziwe kuyambila lero, yeah
udziwe kuyambila lero, yeah
zonsezi ndi zako, zako, zako
mtimawu ndi wako, wako, wako
ukamagona usiku wa lero, yeah
udziwe kuyambila lero
[bridge]
chikondichi ndi chako, baby iwe
mtimawu ndi wako
kuyambira lero
kuyambira lero
udziwe kuyambila lero
[chorus]
chikondichi ndi chako, chako, chako
mtimawu ndi wako, wako, wako
udziwe kuyambila lero, yeah
udziwe kuyambila lero, yeah
zonsezi ndi zako, zako, zako
mtimawu ndi wako, wako, wako
ukamagona usiku wa lero, yeah
udziwe kuyambila lero
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu tim'm west - again
- lirik lagu maraví - no se trata de mí
- lirik lagu hnos ventura - día de la madre
- lirik lagu brishav - simba
- lirik lagu volker rosin - begrüßung
- lirik lagu georgi - darker
- lirik lagu p.candi - bookoo
- lirik lagu mysterio - no money
- lirik lagu laflamme - i hear noise
- lirik lagu kapan - yavaş yavaş