
lirik lagu kelvin sings & beracah - ndekha
[intro: kelvin sings]
mmh mh
[verse 1: kelvin sings]
mawu akewo ndi nyali eya
njira yangayi atsogolera
ndikasunthira kutali eya
kufupi naye amandikokera
he never sleeps sawodzera
nthawi zonse andiyanganira
bwezi langa londikonda yesu yeah, yeah
[chorus: kelvin sings]
sindidzayenda ndekha
ayayaya yeah, yeah
sindidzayenda ndekha
ayayaya
never walk alone
[verse 2: beracah]
away for the whispers and lies that he’s not for me
he’s true to his word what he says he fulfills it
he never sleeps yeah sawodzera
nthawi zonse andiyanganira
bwezi langa londikonda yesu yekhayo
[chorus: kelvin sings & beracah]
sindidzayenda ndekha
ayayaya yeah yeah
sindidzayenda ndekha
ayayaya
never walk alone
sindidzayenda ndekha
ayayaya yeah yeah
sindidzayenda ndekha
ayayaya
never walk alone
[bridge: beracah]
ndidzakamira inu tate
poti mawu anu ndi nyali yanga
ndidzakamira inu tate
poti mawu anu ndi nyali yanga
[chorus: kelvin sings]
sindidzayenda ndekha
ayayaya ayaya yeah, yeah
sindidzayenda ndekha
ayayaya
never walk alone
sindidzayenda ndekha
ayayaya ayaya yeah yeah
sindidzayenda ndekha
ayayaya
never walk alone
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu vic spencer - wax paper/iron
- lirik lagu w0rsty - снова (anew)
- lirik lagu faint⋆star - destruction
- lirik lagu $amaad - only fearing one
- lirik lagu pulkxt - blackout
- lirik lagu lkdr - konfetti im kopf (club extended)
- lirik lagu riff wood - inside out brain
- lirik lagu boredpic - noway
- lirik lagu scence - alone
- lirik lagu miel de montagne - tout tout