lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu kell kay - in love

Loading...

[verse 1: teddy mw]
umangofuna tizicheza
paja umati ndimakuseketsa
tikamayenda kwa milesa
anthu amangotisekelera

[chorus: teddy mw]
am i really in love with you?
pena umangodipepelesa
am i really in love with you?
pena umangodipepelesa

[verse 2: kell kay]
sindingakugawane ndi wina
kodi mawu aku lonjeza
nanga utaponda polakwika
ungadiuze ndisamale?
zomaswerana mtima
kundiuza ndiyiwale
ku lonjeza zosatheka mulibe mwako mu dikishonale
remember utagwada kuti ndidalire
unkati udzandikwatira kuti ndi dikirebe

[chorus: kell kay & kambwiri sisters]
are you really in love with me?
olo uk~mangodipepelеsa
are you really in love with mе?
olo nawe ukunditayitsa
are you really in love with me?
olo uk~mangodipepelesa
are you really in love with me?
olo nthawi ukunditayitsa
[verse 3: teddy mw]
chikondi chako
sindichiwona baby momwe uchikambira
chimandi talikira
ndipo mawu anga wako
amangosintha baby wakhumbira
ine nkhawi bii!!!

[chorus: teddy mw, kell kay & kambwiri sisters]
are you really in love with me?
olo uk~mangodipepelesa
are you really in love with me?
olo nawe ukunditayitsa
are you really in love with me?
olo uk~mangodipepelesa
are you really in love with me?
olo nthawi ukunditayitsa

[outro: kambwiri sisters]
(umangodi umayi)
(umangondipepelesa)
(umangodi umayi)
(umangondipepelesa) are you really in love with me?
olo uk~mangodipepelesa
are you really in love?
olo uk~mangodipepelesa
are you really in love?


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...