lirik lagu jeg tellem - mtopola
ah hee
ah hee
ah hee
yeah hee
mukukamba zinkhani zambiri
mukafuna ndiwononge mbiri
kodi nchikondi
ndimayesa tilimo awiri
muli ndi nthawi muli busy
chonde msachimwise
ayi nsadanise
ndi w~ng~yu
achuluka anthu okhomelela ahahaha
kankhani pang’ono kukhomelela koma why
ati ndingofuna ndingokudyela ineyo
atumapo anthu kuzandikwenya ndee
tinamenyana
mumvetse
olo mu dameje dameje
k~muleka sizingatheke
ndimadana ndi mtopola
muleke
zomakamuwuza miseche
ndicholinga choti athese
ndimadana ndi mtopola
ine ndimadana ndi mtopola
mtopola eh mtopola
mtopola eh mtopola
ndimadana ndi mtopola
ndati ndimadana ndi mtopola
mtopola eh mtopola
mtopola eh mtopola
ndimadana ndi mtopola
yeah
umaganiza bwanji kukwatira beast
iweyo ndi ka beauty ofunika prince
mamuna oti nthumba anathila yeast
osati kafinyanya wonunkha gilisi
mhuu koma mtopola
ndizamumveso wina nzamunokola
k~mawuza anzake andisomphola
ndizamponda pamutu ndi chigogoda
cell nzalowa bola ndamtchola
eya pezani zina zochita
eya kupeza wanu nzovuta
eya mungomupempha chauta
osativuta
mwachuluka anthu okhomelela
kankhani pang’ono kupemelela
ati ndingofuna ndingokudyela
koma tizamenyana
mumvetse
olo mu dameje dameje
k~muleka sizingatheke
ndimadana ndi mtopola
muleke
zomakamuwuza miseche
ndicholinga choti athese
ndimadana ndi mtopola
ine ndimadana ndi mtopola
mtopola eh mtopola
mtopola eh mtopola
ndimadana ndi mtopola
ndati ndimadana ndi mtopola
mtopola eh mtopola
mtopola eh mtopola
ndimadana ndi mtopola
olo mu dameje dameje
k~muleka sizingatheke
olo mumuwuze miseche
yeah ey yeah
yeah ey yeah
ndimadana ndi mtopola
mtopola eh mtopola
mtopola eh mtopola
ndimadana ndi mtopola
ndati ndimadana ndi mtopola
mtopola eh mtopola
mtopola eh mtopola
ndimadana ndi mtopola
mtopola eh mtopola
mtopola eh mtopola
ndimadana ndi mtopola
mtopola eh mtopola
mtopola eh mtopola
ndimadana ndi mtopola
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu elsie zel - interstellar
- lirik lagu nasmore - when will i learn
- lirik lagu lg malique - 100 days
- lirik lagu schäffer the darklord - re-entry
- lirik lagu enkaff - bloodflow
- lirik lagu jake novak - bad gun
- lirik lagu schäffer the darklord - the drummer
- lirik lagu giovane werther - mi hai fatto mare
- lirik lagu itskidjj - for the night
- lirik lagu almendra del pilar - enciende el alma