lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu jeg tellem - dolo ?

Loading...

tellem !!
(jeg)
ah okay , listen up yeah
yeah wawa madolo
yeah inde madolo
yeah sure madolo
yeah zowona dolo
iwe ndi dolo eti ?
uyonso ndi dolo eti ?
nanunso madolo eti ?
chaka chino dolo ak~mana ndi ? {ok}

masiku ano ase, aliyense ndi shasha ase
akangokhala nzako amatha ase
pansi pa mtima wapaka ase
iwe ndi dolo eti ? (dolo)
uyonso ndi dolo eti ? (dolo)
nanunso ma dolo eti ? (dolo)
chaka chino dolo ak~mana ndi dolo

see iyiyi ndi verse one
kwa omwe timabowa delete it pepani
yah tasinkhasinkhani
ku malawi mashasha panopa si nkhani
poti nzeru zawo anangomwera madzi
nde amapopana olo akupanga nyasi
amazimva hip hop akagula vans
tikathoka ngamo atidyesa runs
ati poti mumachila , dolo
poti ndi homie nde amak!lla , dolo
amakudabula ndi priscilla,dolo
basi ma swazi nk~masilila , dolo
mhuu aaah , pali udolo
wina ukapolo
udolo sapangila pakh0m~ pa makolo
kubwereza 4 umenewo nde udolo
osamapanga udolo opanda tsogolo

masiku ano ase, aliyense ndi shasha ase
akangokhala nzako amatha ase
pansi pa mtima wapaka ase
iwe ndi dolo eti ? (dolo)
uyonso ndi dolo eti ? (dolo)
nanunso ma dolo eti ? (dolo)
chaka chino dolo ak~mana ndi dolo

verse two nde madolo ndabweraso
olo mitengo dolo poti abelaso
apalamule olo court inkweraso
atulukaso ndiye tivutikaso
dolo wa hustle nde anayela mmaso
sazatha fasho ngati jada ndi kachaso
mwamatamaso dolo akweza bundle
muwaonaso apasana mipando
nde zika mg~ya
amalowa mu elz or blantyre
kufuna kuzakopa ma bayala
kuyamba kuwapopa ndi vampire
ah shupit, pali udolo
wina ukapolo
udolo sapangila pakh0m~ pa makolo
kubwereza 4 umenewo nde udolo
osamapanga udolo opanda tsogolo

masiku ano ase, aliyense ndi shasha ase
akangokhala nzako amatha ase
pansi pa mtima wapaka ase
iwe ndi dolo eti ? (dolo)
uyonso ndi dolo eti ? (dolo)
nanunso ma dolo eti ? (dolo)
chaka chino dolo ak~mana ndi dolo

dolo , dolo
dolo , dolo
dolo, dolo, dolo
dolo,dolo, dolo
do do do dolo , dolo , dolo
dodododo dolo , dolo ,dolo


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...