lirik.web.id
a b c d e f g h i j k l m n o p q r s t u v w x y z 0 1 2 3 4 5 6 7 8 9 #

lirik lagu isaac liwotcha - siyani nkhondo

Loading...

“[verse]
dziko lapansi anthu akufa ndi nkhondo
ku somalia anthu adafa ndi nkhondo
ku mozambique anthu adafa ndi nkhondo
dziko la kosovo anthu adafa ndi nkhondo

“[verse]
ku pakistani nakonso adafa ndi nkhondo
ku ethiopia nakonso adafa ndi nkhondo
dziko la angola ndithu adafa ndi nkhondo
tipemphe kwa mulungu ufulu
nkhondo ilekeke

“[chorus]
siyani nkhondo tiyeni tiyanjane
anthu osalakwa akufa ngati nsomba
siyani nkhondo tiyeni tiyanjane
anthu osalakwa kufa ngati nsomba

“[verse]
nkhondo iwononga miyoyo
bwanji mukuyikonda
anthu akusowa pokhala
kuvutika kowopsya
tsiku ndi tsiku anthu akufa ndi nkhondo
atiyanjanitse ndi ndani
ambuye thangatani
“[verse]
tipemphe kwa mulungu ufulu
m’mayiko aamzathu
mulungu ayanjanitse onse
aleke k~menyana
tumuzani mzimu wanu mbuye
ku dziko lapansi
anjelo asef~kire konse
alandise nkhondo

“[chorus]
siyani nkhondo tiyeni tiyanjane
anthu osalakwa akufa ngati nsomba
siyani nkhondo tiyeni tiyanjane
anthu osalakwa kufa ngati nsomba

“[chorus]
siyani nkhondo tiyeni tiyanjane
anthu osalakwa akufa ngati nsomba
siyani nkhondo tiyeni tiyanjane
anthu osalakwa kufa ngati nsomba

“[chorus]
siyani nkhondo tiyeni tiyanjane
anthu osalakwa akufa ngati nsomba
siyani nkhondo tiyeni tiyanjane
anthu osalakwa kufa ngati nsomba


Lirik lagu lainnya:

LIRIK YANG LAGI HITS MINGGU INI

Loading...