
lirik lagu isaac liwotcha - musalire
“[verse]
ndidaona (zodabwitsa)
panthawi (yamavuto) oh mama
akuchikazi (adatenga)
katundu yense (ndi ana omwe) oh mama
bambo awo (akali moyo)
koma ana onse (adawalanda) oh mama
ana asowadi (chikondi)
akhalangati (akapolo) oh mama
“[verse]
mukadatenga (katundu yekha)
sichikanakhala (chovuta) oh mama
koma mwatenga (ndi ana omwe)
kuwaika mgulu (lakatundu) oh mama
ana w~nga ndithu (akuvutika)
pamene ine (ndilipo) oh mama
nthawi zonse (ndimangolira)
kulilira (ana w~nga) oh mama
“[chorus]
ana anga musalire
maloto akundivuta ah
mtimawu sukondwela
kuti muvutike eh
ana anga musalire
maloto akundivuta ah
mtimawu sukondwela
kuti muvutike eh
“[verse]
mbuye mverani (kulira kw~nga)
magazi anga (akuvutika) oh mama
mtima w~nga (umafuna)
nditamakhala (ndi ana w~nga) oh mama
koma poti (adandilanda)
ana w~nga (amangolira) oh mama
abambo wathu (ali kuti?)
inu agogo (mutipelekeze) oh mama
“[verse]
ana anga (mudzipemphera)
ambuye amamva (mapemphero) oh mama
musade nkhawa (ambuye alipo)
ndiye adziku (tetezani) oh mama
nthawi zonse (mukamalira)
mtima mw~nga (chisoni) oh mama
ndipempha mbuye (namalenga)
kuti aku (yang’aneni) oh mama
“[chorus]
ana anga musalirе
maloto akundivuta ah
mtimawu sukondwela
kuti muvutike eh
ana anga musalirе
maloto akundivuta ah
mtimawu sukondwela
kuti muvutike eh
Lirik lagu lainnya:
- lirik lagu $not - la tradito
- lirik lagu magik markers - american sphinx face
- lirik lagu billy bats - gros cailloux (remix)
- lirik lagu waze rrx - hero of the day
- lirik lagu штадт (stadt) - стеклянная пыль (the glass dust)
- lirik lagu xxavv - kiss and tell booth
- lirik lagu jamal gasol & vic spencer - the last one
- lirik lagu los compitas de durango - ojitos bonitos
- lirik lagu smoker - ils kiffent tous
- lirik lagu jad fair - why